
ace dirty, krazie g & 60 grxmz - wakutowa lyrics
[intro: montell fish]
talk to me, why don’t you
talk to me? like you used to, you don’t—
talk to me, why don’t you
talk to me? like you used to, you don’t t
[chorus: ace dirty]
mwanakazi wakutowa (horus dem baad)
ndi mafuna ntakushowa
chikondi ndichosowa
ndimangophakira kabowa
ndinagrower ndikublowa
panopa tinalowa
[post+chorus: krazie g]
kwichi, kwichi izi ndi zapabedi pakachoka iwe pakulowa mula
kwichi, kwichi izi ndi zapabedi pakachoka iwe pakulowa mula
[verse 1: 60 grxmz]
ain’t holdin’ grudges my heart cold, don’t wanna talk (f+ck)
my life a movie smokin’ tupe when i’m alone
sled from the bush ndine dolo mario bro
ndukatrapa parcel ku speed pa city mall (mdubz n+gga)
now she sad mix amandiwonawona
h+lla backshot tachita kugwira khoma
she’s always like “baby ndimakusowa”
sakuziwa wandikwana sister wake ndishowa
akufuna banja koma ine ndikufuna ndrama
akufuna mwana koma ine sindimupatsa
wayipelekera ntafuna nditha kuthawa
akufuna banja koma ine ndikufuna ndrama
[chorus: ace dirty]
mwanakazi wakutowa (horus dem baad)
ndi mafuna ntakushowa
chikondi ndichosowa
ndimangophakira kabowa
ndinagrower ndikublowa
panopa tinalowa
[post+chorus: krazie g]
kwichi, kwichi izi ndi zapabedi pakachoka iwe pakulowa mula
kwichi, kwichi izi ndi zapabedi pakachoka iwе pakulowa mula
Random Lyrics
- lawert - пазл (puzzle) lyrics
- sunk1st - mtf (male to fujoshi) lyrics
- jumex - lilliana lyrics
- kamiyada+ - runaway lyrics
- hash! (hashim saeed) - inspire me lyrics
- tyno got it - uncle drive lyrics
- erotic suicide - get what you pay for lyrics
- idjit - dark woods lyrics
- tropacana hermez - 2500 t-shirt lyrics
- operatic - forget + think + tell lyrics