alick macheso - impfa nimulandi lyrics
[intro: jonas kasamba]
yeeeeeeh! chesology!
[chorus: al!ck macheso]
impfa nimulandi, nimulandi
inandilanda, kundilanda makolo anga
impfa nimulandi, nimulandi
inandilanda, kundilanda makolo anga amayo
[verse 1: al!ck macheso]
impfa ndikawalala, inandibera
nzanga w+nga, +n+li wachikondi
impfa ndikawalala, inandibera
nzanga w+nga, +n+li wachikondi mayo
[verse 2: al!ck macheso]
anzathu impfa nimulandi, ndithu inatilanda
kutilanda achibwenzi wathu
anzathu impfa nimulandi, ndithu inatilanda
kutilanda anzanga, achibale amayo
[verse 3: al!ck macheso]
impfa siyisankha, khuti uyu ndiwandani imangotenga chabe
impfa siyisankha, khuti uyu ndiwandani imangotenga chabe amayo
[verse 4: al!ck macheso & elton muropa]
liwa ndomoyipi, ekuelingaa, eyi+elinga, golongani nanga
liwabi khumba+khumba, eyi+elinga, eyi+elinga, golongani nanga
(al!ck)
[verse 5: al!ck macheso]
impfa nimulandi anzanga, inandilanda, inandilanda
kundilanga mwana w+nga, omwe ndinabala kundisiya nandilira amayo
anzanga impfa nimulandi, inandilanda, inandilanda
kundlianga munzanga w+nga, +n+li wachikondi
kundisiya chocho
impfa nimulandi amayo, nimulandi ndikawalala
kutilanda makolo athu, omwe anatibala, kutisiya natilira atatee
chabwino makolo athu, mupume muntendere, (k+mwamba muliko mkomwe mukonze malo athu iiyii+yii+yii oooh+aaah!)
chabwino amayi anga mupume muntendere, (k+mwamba muliko amayo mukonze malo anga iiyii+yii+yii oooh+aaah!)
[verse 6]
[?]
Random Lyrics
- corinhos evangélicos - que povo é este? lyrics
- kussani (rus) - картина (picture) lyrics
- nc1 - bad bitch lyrics
- maz b - release lyrics
- cătălina solomac - demons lyrics
- zemine rehimova - ad günü lyrics
- sunrest - tired eyes lyrics
- maribou state & andreya triana - all i need lyrics
- lil wave (rapper) - climate lyrics
- bryan andreose - tropics lyrics