azlyrics.biz
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

base cube – kuli kashi lyrics

Loading...

[intro: base cube &crispy malawi]
ya
yeah you know
hhee malawian
mmmh
yeh, yeh, yeh, yeh, yeh, yeh, yeh, yeh
(ziwerenge)
(ziwerenge)

[verse 1: crispy malawi]
back then, tikuyamba sizinali chonchi tinkangofuna kuheater
pano tinapita
ndizopita kuti timangopita
kufika ngati wa waterboard loza komwe kuli miter
nfuna kudrippa
been soft for so long, nthumba mw+nga ndikungofuna kulimba

[hook: crispy malawi]
loza kuli cash ase
loza kuli cash ase
loza kuli cash ase

[verse 2: crispy malawi]
spe uli cold ngati ice cube
bt kulinka ndi base cube
views kukwera pa youtube
kuplacker zozunguza mutu
dm kwadzaza tinkhuku, utha kusokoneza ndi kududu
olo utaseka mmakutu, unayamba kundimva gwamba ali duntu
back in ‘018, sanavaye ku area 18
before i lost my queen, rap isanayembe kupayer rent
mmutu w+nga muli tint
nsaku runner komwe business
ma g.o.a.t akupempha ma remix
i had to go and figure it out myself, sungandipusise
[hook: crispy malawi]
loza kuli cash ase
loza kuli cash ase
loza kuli cash ase

[verse 3: base cube]
yah, mvera
ndalama zimatikonda, ndkasanja ndimakondwa
kukhala mmaluzi ukapolo ase, i wanna be freed ngati honda
chilichonse timabosha
look here we ain’t got sh+t on our shoulders
but you know that am looking for frag now, man i don’t even need a poster
yah you know that we keep it a hundred, sitidanda tikapeza fifty
timathamangisa zima business ngati tamva kubwera a city
ooh yah they callin’ me a big dawg, ambirinu mumanditcha biggy
ndkupanga zindalama zangazanga ndimatchila ndi achina pisky
ndimatchila ndi achina crispy
pachi weekend, tikusokoneza
ma guy ambiri amazipopa kaa, ifeyo timangobooleza
ifey timangobwera kutenga zi cash kutenga zi dollar
koma ndi mbola mmm
chif+kwa nde tima baller, eyy

[hook: base cube, crispy malawi & base cube]
loza kuli cash ase (eyy)
loza kuli cash ase
loza kuli cash ase (eyy, iwee)
[outro: base cube]
malawian



Random Lyrics

HOT LYRICS

Loading...