brainlock t-kas & nkhiwa - themba ndi themba lyrics
[chorus : brainlock t+kas]
amayesa kuti ifeyo ndi mphwemphwa
anangodabwa ndangofika ndikubhebha
trap yathu sungalowe chif+kwa siwe member
iyi ndi yama shatta ndi themba ndi themba
amayesa kuti ifeyo ndi mphwemphwa
anangodabwa ndangofika ndikubhebha
trap yathu sungalowe chif+kwa siiwe member
iyi ndi yama dada ndi themba ndi themba
[verse 1: brainlock t+kas]
huh!
themba ndi shatta themba ndi don dada
themba ulemu amalandira ku lusaka
amamufila mu ghetto anthu amamusata
mumapusisana mukamati samatha
themba pa den amamutchula mbwindi
themba nkazi wake ndiwo phula ndichi big
themba ndi wavhifumu k+ma samadya kings
themba ghetto yinamudya koma looks ya dings
tikufuna themba! tikufuna drip!
ukawona themba ndekuti wawona cheese
themba ndi good boy themba ndiwamu street
themba boys yake sizamva ayi
[verse 2: nkhiwa]
themba themba thеmba ndi big stepper
themba thеmba themba ndi big dripper
mukapanga za themba mutsegula mmimba
mukafuse mbali zakwanu themba anthu amamuziwa
themba ndi wachilokolo koma amaziwa style
sungamuyike mu botolo themba ndiwamakani
themba be the reason nkazi wako sakuyankha
machesi ali ndi ife nde themba amangoyaka
uuh uuh boys yake sizamva ayi
themba anachotsa mantha walayi
themba ndichi og themba sichi mphwemphwa
themba sanena odi kwanu tizagenda
[chorus : brainlock t+kas]
mmh yeah
amayesa kuti ifeyo ndi mphwemphwa
anangodabwa ndangofika ndikubhebha
trap yathu sungalowe chif+kwa siwe member
iyi ndi yama shatta ndi themba ndi themba
amayesa kuti ifeyo ndi mphwemphwa
anangodabwa ndangofika ndikubhebha
trap yathu sungalowe chif+kwa siiwe member
iyi ndi yama dada ndi themba ndi themba
Random Lyrics
- caos! (esp) - ella lyrics
- cutiki - pique lyrics
- onlyoneof - give me the love, bitxx lyrics
- little wings - what from the sky lyrics
- the pamphlets (ua) - pochekai lyrics
- rapb0y - the good, the bad and the chupa cool lyrics
- elle baez - i love my body lyrics
- burnt rice - anxiety attack lyrics
- z1x1s - асмод3й (asmodey) lyrics
- žalvarinis - gaudė vėjai lyrics