azlyrics.biz
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

crispy malawi & brainlock t-kas - mkazi wa trappa lyrics

Loading...

[intro : brainlock t+kas]
ayo+
mtima ukungogunda
mtima ukungogunda
mtima ukungogunda
ayo landie (ungogunda)
yah

[chorus: brainlock t+kas & crispy malawi]
the way she love me zachilendo
kavala bandana kandipeza pa bando (yeah)
kali cool ndima frenzo
kamatha ku mixer ndi kupota mtondo
mkazi wa trapper
iwe ndi mkazi wa trapper
mkazi wa trapper (kas)

[verse 1 : brainlock t+kas]
mkazi wa trapper w+ngoposter lero (uh huh)
she was holding a blunt zinamubanda yeyo (huh) (woah)
mkazi wa trapper ndi ka gangster girl (uh huh)
ndika snake ndika slime (uh huh), kangovalaso belo (huh) (oh ho)
mkazi wa trapper ndi trapper
mkazi wa trapper ndi slime (slatt)
akati abwera m’mawa kadya ma blunt nine (nine)
kafuna kuvaya mawa ati sinkhala online (nah)
mkazi wa trapper amachena amakonda nike (yea)
yeah
[chorus: brainlock t+kas & crispy malawi]
the way she love me zachilendo
kavala bandana kandipеza pa bando (yeah)
kali cool ndima frenzo
kamatha ku mixer ndi kupota mtondo
mkazi wa trappеr
iwe ndi mkazi wa trapper
mkazi wa trapper

[verse 2: crispy malawi]
mkazi wa trapper ndi wo trapper mtima (mmh hm)
hotel standard wefu wefu, siza m’chimanga (m’chimanga)
sizongochoka kwanu mk+mati ndimaka (no)
sungandibele olo utakhala ndi mkaka (bwoo)
kakufuna ma kiss, netflix and chills
tikusuta ma cheese, kakamayenda sungakayimitse
makape kakati ka disse, ndichi mponela ngati madise
kama sipaso zima baby gin (gin, gin, gin)
kali ndi kas koma ndine amene ndiku kapanga

[outro : brainlock t+kas & crispy malawi]
zachilendo
ndikupota mtondo
mkazi wa trapper
iwe ndi mkazi wa trapper
mkazi wa trapper
iwe ndi mkazi wa trapper
mkazi wa trapper
mtima ukungogunda
mtima ukungogunda



Random Lyrics

HOT LYRICS

Loading...