
crispy malawi - ace ndi phin lyrics
[intro:]
ayo landie
69 grams, 60 grams
mario brrrrr
ace dirty
mario brrrr (ayyyyy)
achina spee
achina spee
[chorus]
ndufuna cake ndi cream
kuphaka life ndichi team
ndili ndi ace ndi phin
sungatisinthe momwe tililimu
ndufuna cash aseee, ukuti chani
it’s for the gang, rest in peace to vatycan
ukuti bwanji ase ndili ndima guyz
kafusefuse ma fans kuti amafeela ndani
[verse 1: spe, ace]
ndafaka flag ku ghetto, ma kicks ngati chiukepo
nkavala shop ndi mlw drip f+kwa deal ndi bh+llo
kuphusha dancehall pa easy siza pressure
if numbers don’t lie sizofunika ku qwesha
kuyima pa stage promoter kuti payer
iwe ukayima pa stage ndekuti uli pa kameza
ndizolembalemba ngati ma tatoo angawa
amazembazemba anayamba kuthawa
ndinene bwanji kuti ifeyo tinapitilira
ndikhale bwanji koma akuti tuwayimilira
i can do this with my еyes closed kuyisinzinila
ndili pa top, high spliff ndachita kuyithimisila
[chorus:]
ndufuna cake ndi crеam
kuphaka life ndichi team
ndili ndi ace ndi phin
sungatisinthe momwe tililimu
ndufuna cash aseee, ukuti chani
it’s for the gang, rest in peace to vatycan
ukuti bwanji ase ndili ndima guyz
kafusefuse ma fans kuti amafeela ndani
[verse 2: 60 grams]
ndikufuna cash aseh, n+gga want some bandz
a solo blunt is self care, uzi…. ndima grams
ndangovalaso vans ndukatrappa contraband
ndingozidyesa ma swaz ukuziwakale plan
[chorus:]
ndufuna cake ndi cream
kuphaka life ndichi team
ndili ndi ace ndi phin
sungatisinthe momwe tililimu
ndufuna cash aseee, ukuti chani
it’s for the gang, rest in peace to vatycan
ukuti bwanji ase ndili ndima guyz
kafusefuse ma fans kuti amafeela ndani
[outro:]
ayo landie!
69 grams!, 60 grams!
mario brrrrr!
ace dirty!
mario brrrr! (ayyyyy)
achina spee!
achina spee!
Random Lyrics
- seriyouse - the eld3r scroll lyrics
- the damnwells - wreck you lyrics
- miki jevremović - razbiću noćas mandolinu lyrics
- unyluv - сучка из азии lyrics
- kosma król - miał być grime lyrics
- g kuru & onem cool beats - corazón púrpura lyrics
- signature by sb & bhalwaan - gal kurey lyrics
- the nelons - sweet peace lyrics
- princewhateverer - ms. pinkie pie lyrics
- 16campa - ventana lyrics