crispy malawi - angobwerabe lyrics
[intro]
f+f9ine
[pre+chorus]
ma babe ambiri man angobwerabe
43, chimaliro , nyambadwe
ena ali single ena umake
ali ndi a eniake
ali single ngati ali ku party
[chorus]
ali single ngati ali ku party
akufila ati tik+mane
sitik+mvana ngati sitingadyane
ofila dancehall sangamanyade
[verse 1]
nnamukwera kale sanganditsike
ati ali ndi guy oti sangamu cheaty
ex w+nga wina anagwidwa ndi dj
koma ntafuna nditha k+mu caller kuti ndimu+
k+mudeleter ngati amangooneka bho pa ma pictures
ama roller ndi adani k+mawauza kuti andidisse
nnangoziwa kuti si level basi k+mandipanga compare ineyo ndi achina piksy
iwe, yachina spe ndi 1 of 1 sungamafananize
sindingakunamize, ngati sufila dancehal sindingakukakamize
nditha kushala nawe koma sindingakhalitse
umuuzenso blesser wako ndikugulisa ma lipha ndi ma t shirt
osamaphwеkesa mission
[pre+chorus]
ma babe ambiri man angobwerabе
43, chimaliro , nyambadwe
ena ali single ena umake
ali ndi a eniake
ali single ngati ali ku party
[chorus]
ali single ngati ali ku party
akufila ati tik+mane
sitik+mvana ngati sitingadyane
ofila dancehall sangamanyade
Random Lyrics
- t.j. - burgerpommes 2 parodie lyrics
- erosive tendencies - understatement - halloween lyrics
- disoc8 - terrifier lyrics
- bonde do forró - será lyrics
- sidney phillips - all on my mind lyrics
- hana hope - unsaid lyrics
- karma & sez on the beat - mere jaisa nai lyrics
- mike mungu - be by me lyrics
- phelix hagan - outro (hoe verder we komen) lyrics
- alldaway dre - forgot about dre lyrics