crispy malawi - ayi zikomo lyrics
[intro]
malawian
ayi zikomo
[chorus]
kudzuka mornaz kugwada pansi kuthokoza jah, jah f+kwa leronso ndadzuka ndi moyo
gratitude is a must ndimawinner ndikangodzuka sindimgaphwekese
ayi zikomo, ayi zikomo
yeah, ayi zikomo
[verse]
sorry ngati zili zapa easy kwa iweyo
kwa ifeyo ndiza hard takulira mu zikh0m+
kwachoka nzako pali malo ngati suk+mvesa ndekuti sunabholeko za after domo
ndimayenda ndi gang koma nditha kuyenda ndekha
ngati pomwe pali abalepo adani ali pomwepo
eish, funa imali wamva? ngati zili zosakhudza cash
zisandikhudze ndakana nono
dollar ya show sikukwana koma umakwana
no thanks, i can’t take the offer, ayi zikomo
i can’t show up at your place f+kwa ukufila ngati aliyense akuyenera ashale konko
mamva zomwe mandi mandinena ndimafuna kuyankha
koma ndikango burner ndimangoti (ayi zikomo)
[chorus]
kudzuka mornaz kugwada pansi kuthokoza jah, jah f+kwa leronso ndadzuka ndi moyo
gratitude is a must ndimawinner ndikangodzuka sindimgaphwekese
ayi zikomo, ayi zikomo
yeah, ayi zikomo
[outro]
zikomo, zikomo, ayi zikomo
Random Lyrics
- sihie - sonpari lyrics
- nct wish - bubble gum lyrics
- metal chupal - not the real chupal lyrics
- vjèze fur - x*x lyrics
- akup - feathers and rain lyrics
- jaxen crow - public service anouncement lyrics
- redshift - nuit noire lyrics
- cryptick - seed/garden lyrics
- phoebe kreutz - bull run beer run lyrics
- street fever - black crown lyrics