crispy malawi - chamba lyrics
[intro]
we ain’t got no time
ayo landie
[chorus]
ndili ndi anzanga tungosuta chamba
koma ndi anzanga sitimangosuta chamba, yea
ndili ndi anzanga tungosuta chamba
koma ndi anzanga sitimangosuta chamba
[post+chorus]
mtima suvala sanza
nde ukavaya shoppin’ uzitha kusankha
ukafuna mkazi wa figure uzitha ku flippa numbers
uzipusher dancehall osamangosuta chamba
[verse 1]
apa homie akundipasa move ya ndrama (cash)
koma ali busy akupota chamba
zomwe amakamba amapanga sangokamba
koma kwawo amati amangosuta chamba (chamba)
anzanga eni eni anandipasa kale ma flowers
amandipilira ku worker nane late hours
spenaldo ndi hero ali ndima super powers
ena anasiya mowa koma ndimkamwa nawo powers
[chorus]
ndili ndi anzanga tungosuta chamba
koma ndi anzanga sitimangosuta chamba, yea
ndili ndi anzanga tungosuta chamba
koma ndi anzanga sitimangosuta chamba
[post+chorus]
mtima suvala sanza
nde ukavaya shoppin uzitha kusankha
ukafuna mkazi wa figure uzitha ku flippa numbers
uzipusher dancehall osamangosuta chamba
[outro]
ndili ndi anzanga tungosuta chamba
koma ndi anzanga sitimangosuta chamba
ndili ndi anzanga tungosuta chamba
koma ndi anzanga sitimangosuta chamba
Random Lyrics
- bardo (uru) - omw lyrics
- darkice - fentanyl lyrics
- poema arcanus - fugitive lyrics
- elastinen - leikkii lyrics
- dwa sławy - ale ten lyrics
- fm-cinco - fotosdepoisdobeck lyrics
- dorian grau - herr doktor lyrics
- taylor swift - sparks fly / message in a bottle lyrics
- brett bell - god with me lyrics
- hjaltalín - love from '99 lyrics