crispy malawi - mwendo lyrics
[intro]
ayo landie
[chorus]
skin smooth koma umafeela nda?
maso ako akuona nda?
makutu ako ak+mumva nda?
tipase mwendo wako tiyendele nawo
kodi ma baby enawa chimakhala chani?
mkazi wabhobho k+mafeela badman (badman)
boys sizamva ife nde ndi amakani
tikhwimise ubale mu dziko muchepe udani (muchepe udani)
[verse]
mwina ndidekhe ndingogula benz
pena ndimaona ngati nthawi ndikubesa
facts ndiyokuti ma baby amachedwesa
koma ukangolinker nawo amayamba kukudekhesa
si jokes yabhoo ngati siikukusekesa
ndi jokes ina ngati yakudusa kuti suk+mvesa
nde time ina zimangofunika kungodekha
time kuyitenga
zomwe umafuna umazipeza
[chorus]
skin smooth koma umafeela nda? (umafeela nda?)
maso ako akuona nda?
makutu ako ak+mumva nda?
tipase mwendo wako tiyendele nawo
kodi ma baby enawa chimakhala chani? (chimakhala chani?)
mkazi wabhobho k+mafeela badman (badman)
boys sizamva ife nde ndi amakani
tikhwimise ubale mu dziko muchepe udani (muchepe udani)
[outro]
we ain’t got no time
Random Lyrics
- mikrowolnovkached - ошорох тедуб ёсв (enif eb lliw gnihtyreve) lyrics
- mavyrmldy - laços lyrics
- noble kareem - young grass lyrics
- lionheart (uk) - prisoner lyrics
- karlsos - death on the am radio lyrics
- keblack - à la vie à la mort lyrics
- yuke - im knowin lyrics
- dray blcvk - play w me (interlude) lyrics
- siimi - what's real lyrics
- yvng frost - trese lyrics