azlyrics.biz
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

crispy malawi - pake lyrics

Loading...

[intro: krazie g & crispy malawi]
tayima kaye tayima kaye tayima kaye tayima kaye tayima kaye
ndinabettera success ndiku winner
ndiku winner ndikupanga rebet
ndilibe ex koma ngandani?ti alipo mwina
(umfila ndani?) amapanga regret
umafila ndani?
hahaha

[chorus: crispy malawi]
ati amafila spe
atha kuyimba nyimbo zonse +n+loweza tape
ndangokhala phee! ndikufuna ndimumvere
fanbase yangodzadza ndi ma babe
boys singasiye kufila spe
simangomvera nyimbo imapanga relate
it’s all love apapa palibepo hate

[post+chorus: crispy malawi]
nde aliyese pamalo pake (pake pake pake pake pake)
aliyese pamalo pake (pake pake pake pake pake)
aliyese pamalo pake (pake pake pake pake pake)
aliyese pamalo pake (pake pake pake pake pake)
aliyese pamalo pake (pake pake pake pake pake)
pake pake
[verse 1 :crispy malawi]
game ili pachi make, chilichonse chili malo mwake
homie sali stuck koma akufuna ndimukankhe
that’s my dawg sangandilume nde sindingam+th+we
olo ntakhala pa zero iwe dollar sindingakukawe
bola when i make it double zisazakuwawe
we’re on the road tikupanga money ngati katangale
si zambiri koma zokwana ine ndi a’bale
i don’t wanna die before i live my dreams
lord knows how bad i wanna make these m’s
ku runner game with a milli on my name
siza drake koma life was never the same
pano ha!

[chorus: crispy malawi]
ati amafila spe (spe!)
(spe!) atha kuyimba nyimbo zonse +n+loweza tape
ndangokhala phee! (phee!), ndikufuna ndimumvere (mvere)
fanbase yangodzadza ndi ma babe
boys singasiye kufila spe
simangomvera nyimbo imapanga relate
it’s all love apa palibepo hate

[post+chorus: crispy malawi]
nde aliyese pamalo pake (pake pake)
pake pake pake pake (aliyese pamalo pake) pake pake pake
pake pake pake pake pake pake pake
pake pa
pake pake pake pake pake pake pake
pake pa
pake pake pake pake pake pake pake
aah!
[outro: krazie g & crispy malawi]
ndinabettera success ndiku winner
ndiku winner ndikupanga rebet (je mapelle spe)
(international spe) yeah
ndilibe ex koma ngati alipo
mwina amapanga regret
yeah
brrr! brrr!
brrr! gang!
brrr! brrr! brrr!
gang! gang! gang!
hahaha
ndilibe ex koma ngati alipo (malawian)
mwina amapanga regret
yeah chilichonse malo mwake?
hahaha wakafila bwa?
ukudziwa kale
aliyese pamalo pake
aliyese pamalo pake
aliyese pamalo pake
aliyese pa+
pako
krazie g



Random Lyrics

HOT LYRICS

Loading...