crispy malawi - wakutuma nda? lyrics
[intro]
ayo, you already know what it is
mmh+mmh+mh (mmh mh)
mmh+mmh+mh (mmh)
[chorus]
wakutuma nda?
wakutuma nda?
nduziwa umandifila koma wakutuma nda?
ukugwedeza bho koma wakutuma nda?
ukundifilitsa koma wakutuma nda?
kuchita kundichenera choncho ufuna kukopa nda?
kuvungire dm pa status, ufuna uwone nda?
chi babe cha bho nde asakhale ngati nda?
ona thako ladhinda (ona thako ladhinda)
[verse]
tivaye ku date, sinduthoka calendar (mmh)
so many fishes in the sea koma sindufuna kapenta (ayi)
ndilawitse koma sindikupempha
she wanna like me l!ck a lollipop eko yogueta
sindingagwe mu chikondi bola kugwera kuchiphedi
nde ubwere pa level tidyetsane high grade
zima thick mama zitha kucholera bed koma boys sizamva nde utha kubwera tipangeso
zikamachitika sitiposter ali ndi boyfriend
low+key kusumana nеw school hyphen[?]
ati spe “you’ve been hеre koma walabwi ngati tay grin” [?]
ndili mkati kulimbana ndi mafphako ndi ma chan chan
low+key you my sunshine, kicks kusintha jackie chan
girls just wanna have fun, jokes ndungomupatsa
ka mwana kakungokhafa, spe angopuffer
tungodya ma zaza, mwendo wandipatsa
[chorus]
wakutuma nda?
wakutuma nda?
wakutuma nda?
wakutuma nda?
wakutuma nda?
nduziwa umandifila koma wakutuma nda?
ukugwedeza bho koma wakutuma nda?
ukundifilitsa koma wakutuma nda?
kuchita kundichenera choncho ufuna kukopa nda?
kuvungire dm pa status, ufuna uwone nda?
chi babe cha bho nde asakhale ngati nda?
ona thako ladhinda (ona thako ladhinda)
Random Lyrics
- nestre - собрал (assembled) lyrics
- chalk circle - n.i.m.b.y. lyrics
- finn m-k - at the same time lyrics
- stefflon don - protect me lyrics
- tisin - escritura de altura lyrics
- death in june & boyd rice - symbols in souls lyrics
- hella savage - cry to your mama lyrics
- kaleb sanders - marlboro man lyrics
- jr. crown & bomb d. - wag kang pa-eut lyrics
- t havoc - reckless lyrics