dirty flo - saletsa lyrics
[intro]
f9ine entertainment
yeah
yea yea yea
timothy got the fire beats no matter what it is
yeah yeah yeah yeah
(yea yea yea yea)
[chorus]
njala ya ndi pinda (yea)
ndadya ma indica (yea)
ndadula phone bwa? (bwa)
huh i’m in the cut
ndafatsa kukupeza, nkhawa yandipeza (peza)
mutu kuvomera, mtima wandiletsa (wandiletsa)
huh yea
njanja (njanja) iwe saletsa
njanja (njanja) iwe saletsa
njanja (njanja) iwe saletsa
huh, huh, njanja ,njanja (njanja) iwe saletsa
njanja (njanja) iwe saletsa
njanja (njanja) iwe saletsa
[verse 1]
mengalenga ana a mlengi tungoyamika[?]
kuphula sin osawopa zoti lil bro akanena
za ine ndiye mwanenadi
koma zanu hmm hmm sindinamve (yea)
ndine mfana ofewa angofuna kulimbana nane (hmm)
i ain’t falling for no hoe ndiziw+nkhe (mmh mh)
moni ndi ulere koma ndafunsa zikuti bwanji? yeah (mmh)
ngati dollar sikukwana ndeti nzako akuyankhire
ati sindingasiye ku dropper ma hit
that’s why they love me alot
but i’mma need more than that
pano si mwayi ndaneneratu [?]
yeah,titha kunjanja limodzi osapondana phazi
yeah,mkazi ukunjanja nayeso kukana pansi (yeah)
baddie kupota baddie (baddie)
ndiphaka onse koma ndifunabe phax
[chorus]
(f+kwa) njala ya ndi pinda (yea)
ndadya ma indica (yea)
ndadula phone bwa? (bwa)
huh i’m in the cut
ndafatsa kukupeza, nkhawa yandipeza
mutu kuvomera, mtima wandiletsa
huh yea
njanja (njanja) iwe saletsa
njanja (njanja) iwe saletsa
njanja (njanja) iwe saletsa
huh, huh, njanja ,njanja (njanja) iwe saletsa
njanja (njanja) iwe saletsa
njanja (njanja) iwe saletsa
[verse 2]
(kudyerera)
kudyerarera
got high high kandilemba
most high +n+lemba
mfana zatentha (zatentha)
yeah
nkhani ya moni pa mbali pa
sindingakuopeni mafana(no) mwandipeza
jah jah wadalitsa (yea)
njanja iwe yamika
mphasa akazima [?]
mmh rasta wamaliza
[outro]
timothy got the fire beats no matter what it is
Random Lyrics
- siostry grabowskie - cała sala śpiewa! lyrics
- taves - eleyele lyrics
- enphamus - 3 eggs inna pot / famous animal freestyle lyrics
- mehdi jahani - delam pishete lyrics
- braća bez gaća - moja rajka lyrics
- echo tides (grc) - receive lyrics
- 由薫 (yu-ka) (jpn) - crystals lyrics
- satin - taghas lyrics
- şarampol crew - savaş başlar lyrics
- kaze - una de ego lyrics