azlyrics.biz
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

eli njuchi - ma ine lyrics

Loading...

anandikonda munthene ndisanabadwe
amkayimba tinyimbo mwanawe utonthole
+n+li pompa nsanayimilire

anandikwawitsa anandiphuzitsa kuyenda
nkhope yanu sinding+yiwale
ng+yiwale ng+yiwale nono
ntchito zanu ndiwulure
ndiwulure ndiwulure (lure)
amayi anga sindingawanyoze
ndili moyo sangamavutike
kachala kanga sindingawatoze
malipiro sindingawamalize
amayi anga sindingawasale
kuchepa komko tikanyemelane
cha m’ma four phee tilangizane
malipiro sindingawamalize
musadabwe khalidwe ndinabela ma ine
kuyankhula maonekedwe kaoneni ma ine
musadabwe thanzilo
ndili ndi mdalitso
palowapo thandizo, zosezo zigwere
ma ine, ma ine
ndisaname timamvana ndisaname timamvaaa!!
ma ine, ma ine
tidzayimba jabulani tidzayimba jabulaaa!!
nzoyamwira kuti ukhale mfumu mkoyambira
ooh nanji ndidwale ndipomwe muwadiwire
oooh oow maso awo
ukawaona muli njira zawo
muli masophenya mwana wawo
kuti zitheke nditengepo gawo
ooh ndipo zithuzi zawo
atandifungatira m’manja mwawo
zimawulura za mkati mwawo
muli chikondi mtimwa mwawo
musadabwe khalidwe ndinabela ma ine
kuyankhula maonekedwe kaoneni ma ine
musadabwe thanzilo
ndili ndi mdalitso
palowapo thandizo, zosezo zigwere
ma ine, ma ine
ndisaname timamvana ndisaname timamvana
ma ine, ma ine
tidzayimba jabulani tidzayimba jabulaaa!!
ma ine, ma ine
ndisaname timamvana ndisaname timamvana!!
ma ine, ma ine
tidzayimba jabulani tidzayimba jabulaaa!!
njuchi
android 16
bexy



Random Lyrics

HOT LYRICS

Loading...