azlyrics.biz
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

eli njuchi - phone lyrics

Loading...

[intro]
(sispence on the board)
ooh, yeah

[verse 1]
these were the words he said
tili mu deport ndisananyamuke
ukadutsa dedza, dzayimbe phone
let me know if you’re gonna be okay
dzayimbe phone
dzayimbe phone
ayi mwanawe basi ndiye kadzipita
ak+makwera usayang’ane m’mbuyo
zikakayenda kwinako don’t forget where you’re coming from
dzayimbe phone
let me know if you’re gonna be okay
dzayimbe phone
dzayimbe phone
ukakafika dzandiyimbilе
map ndzakulondolere
ukakafika dzandiyimbile
incasе ungadzaponde ndele
nthawi yomweyi, mwakula nsanga
[?] i’m gonna miss you chifu’
mwana w+nga moyo ngosavuta kwa okhawo odziwa chauta
zikakafika povuta mvera nkuwuze chokachita
[chorus]
dzayimbe phone
anytime when you feel like you’re lonely
dzayimbe phone
tidzakhale pansi tidzakochane
ndati, dzayimbe phone
let me know if you’re gonna be okay
dzayimbe phone
dzayimbe phone

[verse 2]
mukunkako chonde k+makalimbika
k+makalimba zinthu zikamakafoka
osasintha mtima omadzichepetsa
tizibwana tingapo k+madziletsa
zikakavuta dzatiyimbile
za whatsapp ife ndik+manzele
mamuna samadzipatsa malire
sikuti kungokwiya basi mupakile
tili kuno tikudikira
ndipo kwathu ndikuyamikila
a eli njuchi ndithudi mwakula
nambala ndiyo zikamakakula

[chorus]
dzayimbe phone
anytime when you feel like you’re lonely
dzayimbe phone
tidzakhale pansi tidzakochane
ndati, dzayimbe phone
let me know if you’re gonna be okay
dzayimbe phone
dzayimbe phone
dzayimbe phone, ih, oh+yeah
dzayimbe phone, ih, oh+yeah
dzayimbe phone, ni, oh+yeah
dzayimbe phone
dzayimbe phone
[verse 3]
ndikafika pothodwa ndithudi ndimayimba phone
and then he tells me “son osagonja”
usawapatse chokamba ana
usakondweretse mdani
ukamagona yimba phone
kwa namalenga ndizotheka, imba phone

[chorus]
dzayimbe phone
anytime when you feel like you’re lonely
dzayimbe phone
tidzakhale pansi tidzakochane
ndati, dzayimbe phone
let me know if you’re gonna be okay
dzayimbe phone
dzayimbe phone

[outro]
zikadzavuta ndati dzayimbe phone
ndati zikadzavuta ndithu dzayimbe phone
zikadzavuta ndati dzayimbe phone
ndati zikadzavuta ndithu dzayimbe phone
zikadzavuta mwana dzayimbe phone
ndati zikadzavuta mwana dzayimbe phone
zikadzavuta mwana dzayimbe phone
moti zikadzavuta mwana dzayimbe phone



Random Lyrics

HOT LYRICS

Loading...