azlyrics.biz
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

fredokiss - mukanene lyrics

Loading...

[intro: vinjeru]
mukanene mukanene
kaya akutumani, mukanene
basi

[chorus: bfb]
mukanene mukanene mukanene (mukanene)
mukanene mukanene mukanene (mukathoke)
kaya wakutumani, mukanene (alaa)
kaya wakunamizani, mukanene (shupiti)

yemwe wakutumani, mukanene
akupwetekesani, mukanene
mukanene mukanene mukanene (mukanene)
mukanеne mukanene mukanеne (mukathoke)

[verse 1: fredo]
nde bwelelani mukanene (eh)
mwandikanika k+mene (eh)
kubwela mutabisa nkhope
kuyenda ndi midima ngati mileme (eh)

munabwela ndi ti njomba ka
mpaka kutumiza khobha ka
ghetto simasunga zoba ka
kanene ntchana ali pompa ka
kundisemela chi nyau (nyau)
kubwela ndi ti mihau (hau)
mwak+mba pasi a galu
ngati ma bubu mulibe mawu

mukanene ku mra
you can tell them how i got paid
cause i be hustling all day
nali ndende but i’m okay

i’m on my knees mama drop cry
conversating with the most high
ghetto glory so i won’t die
fake friends wanna know why

can a young king make moves anymore?
i got everybody scared trynna blow my downfall

[chorus: bfb]
mukanene mukanene mukanene (mukanene)
mukanene mukanene mukanene (mukathoke)
kaya wakutumani, mukanene (mukanene)
kaya wakunamizani, mukanene (mukathoke)

yemwe wakutumani, mukanene (mukanene)
akupwetekesani, mukanene
mukanene mukanene mukanene (pick 2)
mukanene mukanene mukanene
[verse 2: fredo]
pitani mukawauze
zamabodza zisandikhuze
ntchana fredo sangaluze (luze)
only weapon is the most high (most high)

mukanene ku police (police)
fredokiss ndiwa peace (peace)
young boss with a business (business)
sindipanga zau tchisi (tchisi)

mukanene ku chipani (pani)
kodi chimakhala chani (chani)
k+mangopeka zi nkhani (nkhani)
kapena mwatha ma plan (plan)

makape busy pa fb (fb)
two eyes but they can’t see (can’t see)
angokupweteketsani (tsani)
angokupepeletsani (tsani)

i’m trynna receive all my blessings (yeh)
i’m binding your spirit of envy (woo)
now i see why you hate me (hate me)
it’s all because god blessed me (bless me)
going through h+ll, devil knocking on my door
close it in his face, i will never sell my soul

[bridge: bfb]

palibe chinthu anzanga, chosatha (tauze aise)
palibe chinthu anzanga, chosatha (palibe)
nkhale ufumu umene, umatha (umatha)
nkhale unyakwawa umene, umatha (most def)

nkhale ubusa umene, umatha (ehe)
nkhale upresident umene, umatha (basop)
nkhale moyo umene, umatha
nkhale chitsulo chimene, chimatha (lets go)

[chorus: bfb]
mukanene mukanene mukanene (mukanene)
mukanene mukanene mukanene (mukathoke)
kaya wakutumani, mukanene (mukanene)
kaya wakunamizani, mukanene (mukanene)

yemwe wakutumani, mukanene (mukanene)
akupwetekesani, mukanene (mukathoke)
mukanene mukanene mukanene (mukathoke)
mukanene mukanene mukanene (mukanene)

[outro: fredokiss bfb]
ghetto makaveli up in this
chi ntchana aise
tizingochimangilila kuchimangilila ukuku, chatuluka aise (hahaha)

malawi’s most wanted (hahaha)
joseph in the bible, anamagidwa
jesus christ was arrested aise
nelson mandela, martin luther, steve bicko

orton chirwa, kamuzu banda, fredo
mafana ose amene ali mkati
mafana ose amene ali mkati
kaya ndi chichiri, maula, zomba

mzuzu, ku ndende, ku rumphi
aliyese amene akuchita kuziwa kuti
aise uli mkati komano aise sukuyenela kukhala mkati
jah guide aise

nthawi yako ikwana aise
ingoyesesa kuti aise mabondo ako uziwa user aise
jah jah amamva aise

[end]



Random Lyrics

HOT LYRICS

Loading...