gwamba - 48 bars for christ lyrics
[intro]
[?]
[verse 1]
yo (yo)
ndifalitsa uthenga aseh, door by door
ndipo sindisiya pompo floor by floor
za mdyerekezi zuyika matope zimazoba izo
ine nkuyenda ndi yesu aseh 4×4
imagine, see i vaya ku+bar just to speak bars for christ
mpaka chamba chayamba kudanda
gwamba we used to be bruhs for life
kulikonse ndingavaye, devil akubwera konko
koma sangandigwire, kutelera ngati sopo
lucifer namva kwa mulungu unkayambitsa nkhondo
koma zima billion sizingalimbane ndi khodo
mr yesu nd+nkanama, singa+prayeh osa blesser
sindingathe dzina lake osalikweza
tsiku silingathe iyeyo osamupembedza
tsiku silingathe iyeyo osanditeteza
man pepani, yehova ndе ndi boss
anachoka k+mwambwa kundifela pa cross
ndimakhala ndi njala amapanga zotheka kuti ndipezе ka bread ndiye ndi achina toast
ndachina hyphen, ndachina maskal
amafilanso zimamfana za danso
koma zapazikozi zilibe ntchito ndimafuna kuzavaya ku paradisò ngati saso
komanso, jehova jireh samafuna zimamfana zimujaile
ndekuti uku a christu akunjoya, asilamu chimodzimodzi, ma ras kufila ayile
[bridge]
ah+ah, sley sinamalize aseh
[verse 2]
listen, yo
struggle m’moyo mw+nga nde ndayiwonako
zochitika zina mpaka kuyambana ndanzako
chisanzo, kuyimba gospel ndi chisankho
koma si anzanga onse amakodwera nacho
hustle, tili ma mfana, timayima mu nsewu
njale zabwino zikadutsa ife kuponya maso
lero mzanga wagula benz
sindukondwa nazo
nduti wayenjeza bola anakagula passo
pamene ndinawona za mziko nzopanda ntchito
aseh mtima pansi just focus on your people
zikayamba kuyenda all they do is panic
+n+lemera mfana uja +n+lowa satanic
amazipopa mfana uja amaziyesa ndani
chani, chani, chani? (chani, chani, chani? koma)
mwa yehova ndi dilu
ndi momwe ine ndimapeza filu
slay, bars for christ
gwambizo got bars for christ
aseh slay, bars for christ
gwambizo got bars for christ, slay
bars for christ
gwambizo got bars for christ
[outro]
[?]
Random Lyrics
- winston sharples - call tobor the 8th man lyrics
- the band in heaven - jean jacket - music television (remix) lyrics
- ace & dj guze - rua da frente lyrics
- nane - din casă lyrics
- troski - zapłon lyrics
- 東京パフォーマンスドール (tokyo performance doll) '2013 - it’s up to me lyrics
- piggy del rey - slumber party (deluxe track) lyrics
- sentino - !ll lyrics
- leviticus - the world goes ‘round lyrics
- na$tyk [kd] - mesientotriste lyrics