gwamba - akondakitale lyrics
[intro: lawi]
yi, aye+iye+yah
aye+iye+yah
[chorus: lawi]
akondakitale ndalama ndalipilayi ndati ndipemphe, mundibwenzereko chenje

ulendo w+nga ukathera ku lilongwe, m’deport
koma ndipemphe, mundibwenzereko chenje
inu ulendo w+nga ukathera ku lilongwe, m’deport
koma ndipemphe, mundibwenzereko chenje, yi
[verse 1:gwamba]
aish, ndalama nde yavuta pa nyasa
daily fans k+mayisaka
sikuwona zoti ndiwe shasha
k+menya business basi k+mayitsatsa
nde mukapeza ka ndalama sister, chonde k+makagwiritsitsa
mukamagona nako kukafunditsa
kwachuluka mbava nde muzikabisa
[chorus: lawi]
yi, ndikupempha mundithandize
yi, w+ngondivuta ndi uphawi (ayi)
ah, ah
akondakitale ndalama ndalipilayi ndati ndipemphe, mundibwenzereko chenje
akondakitale ndalama ndalipilayi ndati ndipemphe, mundibwenzereko chenje
ulendo w+nga ukathera ku lilongwe, m’deport
koma ndipemphe, mundibwenzereko chenje
inu ulendo w+nga ukathera ku lilongwe, m’deport
koma ndipemphe, mundibwenzereko chenje, yi
[verse 2: gwamba]
aish, conductor pokwera umati 100 ndangokhala pansi ukuti 120
aseh, osaziyamba zin+z+
muno sindichoka ngati sundipatsa change
wekha ukudziwa dollar ili pa minga
povaya kudedza pena kukwera njinga
umayesa ngati ukundiyimba
lero lonkha wandilira sindiyimva
[chorus: lawi]
yi, ndikupempha mundithandize
yi, w+ngondivuta ndi uphawi (ayi)
ah, ah
akondakitale ndalama ndalipilayi ndati ndipemphe, mundibwenzereko chenje
akondakitale ndalama ndalipilayi ndati ndipemphe, mundibwenzereko chenje
ulendo w+nga ukathera ku lilongwe, m’deport
koma ndipemphe, mundibwenzereko chenje
inu ulendo w+nga ukathera ku lilongwe, m’deport
koma ndipemphe, mundibwenzereko chenje, yi
[verse 3: gwamba]
aish, komanso yesu akufuna change mama
koma change akufuna iye si ndalama
akufunitsitsa inuyo makamaka mutasintha ndikuyamba k+mutsata
mapemphero ndi hustle ya uzimu
mukapusa tsiku lomaliza, no change
mapemphero ndi hustle ya uzimu
ukapusa tsiku lomaliza, no change
[chorus: lawi]
yi, ndikupempha mundithandize
yi, w+ngondivuta ndi umphawi
ah, ah
akondakitale ndalama ndalipilayi ndati ndipemphe, mundibwenzereko chenje
akondakitale ndalama ndalipilayi ndati ndipemphe, mundibwenzereko chenje
ulendo w+nga ukathera ku lilongwe, m’deport
koma ndipemphe, mundibwenzereko change
inu ulendo w+nga ukathera ku lilongwe, m’deport
koma ndipemphe, mundibwenzereko chenje, yi
Random Lyrics
- retro nicotine - when the summer ends :/ lyrics
- oh brother - halb so wild lyrics
- 神宿 (kamiyado) - orange blossom lyrics
- moscow - 21 (freestyle) lyrics
- ar liu fuyang - hustle 经济学 (hustle economics) lyrics
- leellamarz (릴러말즈) - don't cry lyrics
- raved - схожу с ума (i'm going crazy) lyrics
- yng vant - my way lyrics
- ryan gebhardt - a worried song lyrics
- sex pistols - problems (demo) lyrics