gwamba - final say lyrics
[chorus: dan lu]
ndayimvela kutali ayi sindigonela ine
inu yehova, you’re the final say
matenda angawa ati alibe mamkhwala
inu yehova, you’re the final say
[verse 1: gwamba]
ay, ambiriwa aku+talker
akuti ndili ndi tsoka
ndikamayenda kunyoza
akuti simundikonda
akuti ndilibe chuma
pogona panga pa mphasa
ayiwala mumalanda
mukafuna mumapatsa
tsogolo langa lowala
ndidakalibe ndi hope
muzandichotsa ndikukhala
kukandifikitsa pa top
muzandiveka zovala
muzandichotsa manyazi
muzandipatsa mamkhwala
matenda onsewa m’madzi
[chorus: dan lu]
yehova (you’re the final say)
yehova (you’re the final say)
mwandiwona ndine mwana wanu
(you’re the final say)
mundichotse chitonzo papa
(you’re the final say)
[verse 2: gwamba]
amangowona k+mwamba
zonsezi mukamakamba
ndikapempera amanva
tsiku lina adzayankha
amangowona k+mwamba
zonsezi mukamakamba
ndikapempera amanva
tsiku lina adzayankha
[bridge: dan lu]
zaka zitatu zadutsa osamuwona mwana ineyo
anthu akungoseka, anyogodola ati ndine gocho
koma yehova (you’re the final say)
misonzi yanga ndapeleka kwa inu
chitonzo changa muchichotse ndinu
chimwemwe changa muchiyike ndinu
ambuye ndalira pa dzina lanu
[outro: dan lu]
(you’re the final say)
yehova (you’re the final say)
mwandiwona ndine mwana wanu (you’re the final say)
munchotse chitonzo baba (you’re the final say)
ahoo (you’re the final say)
yehova (you’re the final say)
ahoo baba (you’re the final say)
ahoo baba (you’re the final say)
final say
final say
final say
Random Lyrics
- chikili tubbie - por fin ya veo la luz (bonus track) lyrics
- blaise lucarelli - stay lyrics
- lil tugboat - karma lyrics
- pavel morrow - brain reflection, pt. 2 lyrics
- trueneek - ready for the aliens lyrics
- prince amine - seh lyrics
- landon austin & bailey jehl - i’ll be lyrics
- las aves - tomorrow lyrics
- crown the king - fence lyrics
- parmalee - forget you lyrics