gwamba - mtima pansi lyrics
[intro: onesimus]
(sley)
mm
eh+eh, yeah
tata+lala+ta
[chorus: onesimus]
uyike mtima pansi
usadandawule khala pansi
zonse ndi nthawi basi
usamasweke mtima nzinthu zazing’ono
gwada yehova akugwire nkono
tadekha, tadekha
ah
ooh
[verse 1: gwamba]
uh, gwada kwa ambuye ndi mavuto ako
akafuna kuyankha samafunsa nzako
muwuze zonse zokhumba za mtima wako no
ndiwamkulu heavy kuposa vuto lako, aish
ndiyekhayo yemwe angakukonze
anawolotsa nyanja achina mose
akhale patsogolo nzinthu zonse
olo utachimwa bwanji akudzodze
osadanda mphw+nga izi nzazing’ono
yehova wa k+mwamba ali ndi chisomo
ika manja m’mwamba akugwire nkono (akugwire nkono)to
[chorus: onesimus]
uyike mtima pansi
usadandawule khala pansi
zonse ndi nthawi basi
usamasweke mtima nzinthu zazing’ono
gwada yehova akugwire nkono
tadekha, tadekha
ah
ooh
[verse 2: gwamba]
uh, mwetulira mphw+nga usanyatsitse nkhope
akachedwa kuyankha usatope
umawerеnga bible, ana a mulungu anayenda pansi kwa zaka forty
mlaliki pa guwa kulalikira a gonthi
maso patsogolo iwe si mkazi wa loti
pa nyanja yamachimo upangе float ngati boat
machimo mu mtima mwako kupanga deport
eish, mphepo ya ukali
yawe akugwira nkono ufika kutali
ndati mphepo ya ukali
akayendetsa yawe moyo wako wa utali
[chorus: onesimus]
uyike mtima pansi
usadandawule khala pansi
zonse ndi nthawi basi
usamasweke mtima nzinthu zazing’ono
gwada yehova akugwire nkono
tadekha, tadekha
ah
ooh
Random Lyrics
- bubblegum octopus - perfect again lyrics
- kidz bop kids - achterbahn lyrics
- liam kazar - nothing to you lyrics
- sam butera - skinny minnie lyrics
- xzarkhan - drag radials lyrics
- czerwone gitary - tańczyła jedno lato lyrics
- philly lyrics lyrics
- who-ya extended - call my name lyrics
- vinicius terra - meu bairro, minha língua lyrics
- kaolin - ce matin lyrics