isaac liwotcha - musalire lyrics
“[verse]
ndidaona (zodabwitsa)
panthawi (yamavuto) oh mama
akuchikazi (adatenga)
katundu yense (ndi ana omwe) oh mama
bambo awo (akali moyo)
koma ana onse (adawalanda) oh mama
ana asowadi (chikondi)
akhalangati (akapolo) oh mama
“[verse]
mukadatenga (katundu yekha)
sichikanakhala (chovuta) oh mama
koma mwatenga (ndi ana omwe)
kuwaika mgulu (lakatundu) oh mama
ana w+nga ndithu (akuvutika)
pamene ine (ndilipo) oh mama
nthawi zonse (ndimangolira)
kulilira (ana w+nga) oh mama
“[chorus]
ana anga musalire
maloto akundivuta ah
mtimawu sukondwela
kuti muvutike eh
ana anga musalire
maloto akundivuta ah
mtimawu sukondwela
kuti muvutike eh
“[verse]
mbuye mverani (kulira kw+nga)
magazi anga (akuvutika) oh mama
mtima w+nga (umafuna)
nditamakhala (ndi ana w+nga) oh mama
koma poti (adandilanda)
ana w+nga (amangolira) oh mama
abambo wathu (ali kuti?)
inu agogo (mutipelekeze) oh mama
“[verse]
ana anga (mudzipemphera)
ambuye amamva (mapemphero) oh mama
musade nkhawa (ambuye alipo)
ndiye adziku (tetezani) oh mama
nthawi zonse (mukamalira)
mtima mw+nga (chisoni) oh mama
ndipempha mbuye (namalenga)
kuti aku (yang’aneni) oh mama
“[chorus]
ana anga musalirе
maloto akundivuta ah
mtimawu sukondwela
kuti muvutike eh
ana anga musalirе
maloto akundivuta ah
mtimawu sukondwela
kuti muvutike eh
Random Lyrics
- 5122 - vision lyrics
- sorana - kiss back lyrics
- wardruna - skuggehesten lyrics
- nikos gounaris - για τις γυναίκες ζούμε (gia tis gynaikes zoume) lyrics
- the frowning clouds - the grass is greener (further still) lyrics
- chandler cooper - so long lyrics
- oscar - rags to riches* lyrics
- huxp - こっち向いて baby (look this way, baby) lyrics
- cosmograph - jump up (goddess of victory: nikke original soundtrack) lyrics
- the deer (band) - hawkmoth lyrics