jeff nyimbo - bwinobwino lyrics
[intro]
it’s you that mega
[chorus]
ndili bwin0bwino ndilibwin0bwino
ukapweketsa ine uchotsedwa dzino
ndikupanga dzina dollar kupanga zina
mkazi akatripa tikupeza wina
[hook]
ndili bwin0bwino ndilibwin0bwino
ndili bwin0bwino ndilibwin0bwino
[verse]
ndili bhobho mongasukuwona wekha
tili pompa sitikupita komwe kwa tentha
ukayishosha dziwa kuti sindikubwera ndekha
ukayipa dziwa nyimbo
chi mfana chaku mpanda pa mpanda ku 49
after kubanda tukadya chiwaya mu guliver
tsogolo kuwala kwambiri mafana sakutayima
sindikuyankha ndili busy mwina yesa ku typer
beast pa beat nde ndikubwera ndi yokalipa
ndamuvula beat ukudziwa masiku omaliza
amazimva u gee koma akayamba sak+maliza
moto ndi unadi mukafuna m+th+ kupaliza
fresh to death ndak+mana ndichi richmond
face to face sungalimbane ndi ine
ase ndili bwin0bwino mu dancehall ase
sitilimodzi koma basi kubwata koma ase
[chorus]
ndili bwin0bwino ndilibwin0bwino
ukapweketsa ine uchotsedwa dzino
ndikupanga dzina dollar kupanga zina
mkazi akatripa tikupeza wina
[hook]
ndili bwin0bwino ndilibwin0bwino
ndili bwin0bwino ndilibwin0bwino
it’s you that mega
Random Lyrics
- miley cyrus - doctor (demo) lyrics
- dwp academy feat. d jay - feeli free lyrics
- ary (deu) - ich tu' dir weh (weil jemand anderes mich verletzt) lyrics
- envy (rapper) - juvenile jades lyrics
- nora aunor - don't you believe it lyrics
- empress of - what's love lyrics
- l1mitl0ve - зима (winter) lyrics
- unknown artist - keep it hardcore lyrics
- derusz - it was good until it wasn't. lyrics
- james keelaghan - honoré lyrics