kamarih - zidutswa lyrics
mmh mmh mmh mmh mmh
come on yeah
i heard all about you
koma nd+nkayesa uzasintha ndi chikondi yeah
i just couldn’t face the truth
i chose to be blinded by your body
abale atandiletsa sind’amvere nd+nkayesa angopanga chabe nsanje
oh nsanje angopanga chabe nsanje
anzanga atandiletsa sind’amvere nd+nkayesa angofuna andilande
ah ndilande nd+nkayesa andilanda
pano w+ngosiya zidutswa
zidutswa m’mtima mw+nga
zidutswa m’mtima mw+nga
w+ngosiya zidutswa
zidutswa m’mtima mw+nga
waswa mtima w+nga yeah
no one left here to lean on
no one there to save me i’m going under
i chose you above it all
pano ndaphula zibwana zanga
abale atandiletsa sind’amvere nd+nkayesa angopanga chabe nsanje
oh nsanje angopanga chabe nsanje
anzanga atandiletsa sind’amvere nd+nkayesa angofuna andilande
ah ndilande nd+nkayesa andilanda
pano w+ngosiya zidutswa
zidutswa m’mtima mw+nga
zidutswa m’mtima mw+nga
w+ngosiya zidutswa
zidutswa m’mtima mw+nga
waswa mtima w+nga yeah
Random Lyrics
- øzi (stefan chen) - bleu lyrics
- seff - ненавижу (i hate) lyrics
- ellen krauss - picking up lyrics
- family*5 - i don't care lyrics
- beltrano - memória lyrics
- bloody kondr & under mnp - k-pop lyrics
- msomali - kazi yangu lyrics
- steves j. bryan - kitem ale lyrics
- proderly - aster of a lifetime lyrics
- leonardo visioli - satellite lyrics