azlyrics.biz
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

kell kay - lobola lyrics

Loading...

[intro]
you already know
(tricky beats)

[verse 1]
loved you for a long long time
you’ve been mine for a long long time
kwathu unadzawonekelanso
but in my dreams zonsezi
in my dreams

[pre+chorus]
i love you but i can’t say
i want you but i can’t say
i need you but i can’t say
poti uli ndi wako kale
wa ndalama kale
ali ndi chi thilakitale
komanso ndimawopa ine

[chorus]
vuto ndine singakwanitse lobola
vuto ndine singakwanitse lobola
kandalama kanga ndikochepa
singakwanitse lobola
kandalama kanga ndikochepa
singakwanitse lobola
[verse 2]
is it true what they say
mkazi okongola malawi yonse
ndimbali zinayi zaku uk
atinso usa, oh+ah
anaku controller
anukugulilanso mortal love
singakwanitse olo motorola
komabe umandidolola

[pre+chorus]
i love you but i can’t say
i want you but i can’t say
i need you but i can’t say
koma nalota utandilola
koma lobola inandibalalitsa m’maloto mw+nga

[chorus]
vuto ndine singakwanitse lobola
vuto ndine singakwanitse lobola
kandalama kanga ndikochepa
singakwanitse lobola
kandalama kanga ndikochepa
singakwanitse lobola

[bridge]
in my life you comе first like genesis
my first lovе like a diamond, yeah
i love you but i can’t have you
mthumba mw+nga m’mopanda malo
oh, ndimakukonda koma ndalama ndilibe
oh, ndimakufila koma singakukwanitse
[chorus]
vuto ndine singakwanitse lobola
vuto ndine singakwanitse lobola
kandalama kanga ndikochepa
singakwanitse lobola
kandalama kanga ndikochepa
singakwanitse lobola



Random Lyrics

HOT LYRICS

Loading...