azlyrics.biz
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

kelvin sings - aye lyrics

Loading...

yeah…
alright

ndidzala mawu anu pakamwa pangapa
nditama inu pakusuntha kwa lilaka
manjenje ayi paliponsepo ndiponda
ndiwope ndani poti ndinu ngaka yanga

baba you supply
zonse zomwe ndimasowa
kuyesa kufotokoza
ayi mpaka dzuwa litalowa
everybody knows
baba you supply
zonse zomwe ndimasowa
kuyesa kufotokoza
ayi mpaka dzuwa litalowa

chisomo chanu chandizungulira
oyiwalidwa mwamuk+mbukira
zomwe mumanena ndikhulupilira
ndikhulupilira malonjezo anu mukwaniritsa
ife tingoti

amen aye amen aye
malonjezo anu
amen aye amen aye
mukwaniritsa
amen aye amen aye
all your promises are
amen aye amen aye

aye aye aye aye
all your promises are
aye aye aye aye
all your promises are

ndikhulupira chilichonse mumakamba
pazinkhanira mudzayala gome langa
oh when you say it is well
you never retract
mumalizitsa ntchito yomwe mumayamba

baba you supply
zonse zomwe ndimasowa
kuyesa kufotokoza
mpaka dzuwa litalowa
everybody knows
baba you supply
zonse zomwe ndimasowa
kuyesa kufotokoza
ayi mpaka dzuwa litalowa

chisomo chanu chandizungulira
oyiwalidwa mwamuk+mbukira inu baba
zomwe mumanena ndikhulupilira
ndikhulupilira malonjezo anu mukwaniritsa
ife tingoti

amen aye amen aye
malonjezo anu
amen aye amen aye
mukwaniritsa
amen aye amen aye
all your promises are
amen aye amen aye

aye aye aye aye
all your promises are
aye aye aye aye
all your promises are
amen aye amen aye
all your promises are
aye aye aye aye



Random Lyrics

HOT LYRICS

Loading...