azlyrics.biz
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

kelvin sings - vuto siine lyrics

Loading...

intro

“alright”

(verse 1)
galimoto lamwini wake ife tangotchovela
tasala pang’ono kufika moti tiyambe kuchosela
ndinali mmodzi mwaamene amanyozela
zaukulu wake koma ine unandionekela

mbuye sanandiiwale
sanafune ndichakwale
atandiona anati male
bwela nkusamale

this is not the place for you
i have a better task for you
nanditsuka k-mutu ndi nkuphanzi
ngongole yake ndingalipe bwanji

ndeno ndili pa nsamuko
mwini nyumba walamula
pakakhala mafunso oohh
oyenela kuyenela kuyankhula aah

hook

siine
vuto siine yeah x3
koma zomwe wachita chauta
ndizomwe zandisautsa
vuto siine x3

(verse 2)
man i blame it on you lord
for loving me too much
mwafunisisa ndikafike komwe munandituma
you do whatever it takes baba
to make sure i get a plate baba

pa tebulo yanu
ilo ndilo khumbo lanu
langa ndichite chifunilo chanu
nde mundikuta muchinsalu chanu

mutati mudziwe zimene jehovah wachita paine
mwinaso misonzi ndikhetsayi siyokwanila
anatsuka k-mutu ndi kuphazi
ngongoleyi ine ndingalipe bwanji

nde ndili pa nsamuko
mwini nyumba walamula
pakakhala mafunso
oyenela kuyankhula aahh

(hook)

siine
vuto siine yeah x3
koma zomwe wachita chauta
ndizomwe zandisautsa
vuto siine x3

(bridge)
zomwe mwachita ndizovuta kuiwala
nkona misonzi yachimwemwe ingoyenda pamasaya
poti kunali kotheka
kuti ine mundisiye ndekha
koma mwayalula nkeka
mwati ndisamuke
panthaka yopanda chondeyi
vuto siine



Random Lyrics

HOT LYRICS

Loading...