azlyrics.biz
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

kelvin sings (mw) - manjenje lyrics

Loading...

[intro]
mm, yeah, yah

[verse 1]
ukadzuka m’mamawa nkuyamika yehova (yehova, yah)
nk+mudalira kuti mavuto ako awasowa (awasova)
ebeneza, ndikutali wakuchotsa, yeah, yeah
pakamwa pako matamando osasosa, yah

[chorus]
amakuwopa awa, oh+no+no
amachita manjenje, oh+no+no, no+no, no+no
amakuwopa, awo, yeah, oh+no+no+no
amachita manje+, amanjenjemela nawe

[verse 2]
mavuto opanda kuwapempherera
ndyelekezi akawona zotelezi amasekelela, yeah
akondwera akawona kuti ku tchalitchi watenga tchuti, yeah
m’maganizo sungatsutsike m’mayesero akati alunjike
ukagwadwa ndikupemphera, k+midima k+matekeseka
ukamudziwa namalenga, ndizovuta kutekeseka

[pre+chorus]
poti nkhondo uk+menya pansipo anawina kale yawe
ukasiya kuyenda ndidziko nk+mayenda naye yawe
[chorus]
amakuwopa awa, no+no+no+no
amachita manjenje, oh+no+no+no+no
amakuwopa awo, oh+no, no+no, no+no
amachita manjenje, amanjenjemela nawe

[verse 2]
poti kupempheraku ndi nkhondo (rethe)
adani satopa kuzinga mikondo
pambuyo payesuyo londo
you already know zikavuta ndimagwada pama+
kuyitanila conqueror
nchipululu simokhala
palibe chomulaka
azaveka adani juzi mu october, yeah
you’re royalty, vala chisoti chako
the rest is vanity, iwe izi sizako

[pre+chorus]
poti nkhondo uk+menya pansipo anawina kale yawe
ukasiya kuyenda nk+mayenda naye yawe

[chorus]
amakuwopa awa,yah , no+no+no+no
amachita manjenje, oh+no+no, no+no
amakuwopa, awo, oh+no, no+no, no+no
amachita manjenje, amanjenjemela nawe
[bridge]
akazindikira what the almighty has inside of you
napepe, oyipayo amagwidwa manjenje
napepe, oyipayo amagwidwa manjenje
napepe, oyipayo amagwidwa manjenje

[chorus]
amakuwopa awa,yah , no+no+no+no
amachita manjenje, oh+no+no, no+no
amakuwopa, oh+no, no+no, no+no
amachita manjenje, amanjenjemela nawe

[outro]
amakuwopa, awo (woo)
amachita manjenje (yeah)
amakuwopa awo
amachita manjenje, manjenjemela



Random Lyrics

HOT LYRICS

Loading...