kelvin sings (mw) - zonse lyrics
[intro]
yeh, yeah, yeah, yeah, yay, yeah
[verse 1]
honey iwe zomwe wandimvetsa mtimamu
ayi ne, ne, ne, ne
ayi ne, ne, ne, ne, ah
honey iwe, mtima wakondwetsa honey iwe, iwe
ayi ne, ne, ne, ne
ayi ne, ne, ne, ne, ah
ngakhale nkhawa yaying’ono, ako maso alunjike (kwa ine)
ukusowa chani ‘we, ndiwuze ndikakufikire (patali ine)
[pre+chorus]
poti mwa anzanga onsewa
mwa amuna onsewa palibe mamuna amenе ak+mva ngati ine
palibe, palibe
poti alibе, alibe awa
mphumi ngati ineyo, poti ndinapata
[chorus]
zonse mwa m’modzi
zonse mwa m’modzi
(zonse, zonse, zonse, zonse, yah)
zonse mwa m’modzi
zonse mwa m’modzi
(zonse, zonse, zonse, zonse, yah)
[post+chorus]
ndi m’mene ulili ndithudi ndangoyenera kukutenga
uli ndi + +
(zonse, zonse, zonse, zonse, yah)
ndi m’mene ulili ndithudi ndangoyenera kukutenga
uli ndi + +
(zonse, zonse, zonse, zonse, yah)
[verse 2]
ndi kutali komwe tikulowera, ah
lowera, ah
but knowing that i got you by my side
suddenly everything is simplified
mdima sinzayenda ndekha ine (sungalole iwe)
kukawala sing+yende ndekha ine (singalole ine)
zonse zomwe ndifuna, you got it (plus more)
payiwe ine liwuma, ooh darly (i know)
[pre+chorus]
mwa anzanga onsewa
mwa amuna onsewa palibe mamuna amene ak+mva ngati ine
palibe, palibe
poti alibe, alibe awa
mphumi ngati ineyo, poti ndinapata
[chorus]
zonse mwa m’modzi
zonse mwa m’modzi
(zonse, zonse, zonse, zonse, yah)
zonse mwa m’modzi
zonse mwa m’modzi
(zonse, zonse, zonse, zonse, yah)
[post+chorus]
ndi m’mene ulili ndithudi ndangoyenera kukutenga
uli ndi + +
(zonse, zonse, zonse, zonse, yah)
ndi m’mene ulili ndithudi ndangoyenera kukutenga
uli ndi + +
(zonse, zonse, zonse, zonse, yah)
[bridge]
alright
umamkonda ndani? (ine)
ndimamkonda ndani? (iwe)
nyimboyi ndiyandani? (iwe, iwe, iwe, iwe, iwe)
umamkonda ndani? (ine)
ndimamkonda ndani? (iwe)
nyimboyi ndiyandani? (iwe, iwe, iwe, iwe, iwe)
umamkonda ndani? (ine)
ndimamkonda ndani? (iwe)
nyimboyi ndiyandani? (iwe, iwe, iwe, iwe, iwe)
[chorus]
iwe, yeah
zonse, zonse, zonse, zonse, yah
zonse mwa m’modzi
zonse mwa m’modzi
zonse, zonse, zonse, zonse, yah
[post+chorus]
ndi m’mene ulili ndithudi ndangoyenera kukutenga
uli ndi + +
zonse, zonse, zonse, zonse, yah
ndi m’mene ulili ndithudi ndangoyenera kukutenga
uli ndi + +
zonse, zonse, zonse, zonse, yah
[outro]
ayi ne, ne, ne, ne
ay, yeah
ayi ne, ne, ne, ne, ah
zonse
ayi ne, ne, ne, ne
ayi ne, ne, ne, ne, ah
uli ndi zonse
ayi ne, ne, ne, ne
zonse
ayi ne, ne, ne, ne, ah
zonse
ayi ne, ne, ne, ne
ayi ne, ne, ne, ne, ah
zonse
Random Lyrics
- ekeno - grindin' lyrics
- iradə ibrahimova - yaşananlar lyrics
- afn peso - not hurt lyrics
- boj - your love (mogbe) lyrics
- seksi - cerak ragazzi lyrics
- happy asmara - ilusi ra no pinggire lyrics
- phil ochs - draft dodger rag (live) lyrics
- avelino - me and my friends lyrics
- pedro rivera - la bola negra lyrics
- link lewis - moments lyrics