khevado major,dopekid 808 - sober lyrics
(dopekid 808) hook
suli fly uli sober
am with bois kuphazi titachonga
they tryna be like us ulibe dollar
iwe tachoka iwe tachoka
(khevado major ) vers
ndulondola gvng yakhola phone
kuno kuli bawa paja ndiwe wama best
ma blunts ndima mama kuno nde zimatako
sizikupereka sp+ce zabooka zimatako
ndangovara shirt kuphazi j4
phone ilithumba ndikunukhilasobho
mwasamba ndangat mwakonzeka lets go
juss have fun ngt thumba muli bhoooo
(virmin) vers
hook
(carson) vers
iwe tachokaaaa choka choka choka choka…
ngini yako siimakoma taiphula ndife pano tikuphika (phika phika phika)
osadabwaaa ndizomwe tikupanga
takutuluka mesa umalenga
ndangofika ndapatsidwa double shot
ndangofika ndapatsidwa kale hug
ndangofika sindikudziwa zitha bwanji (eeeh sindikudziwa zitha bwanji)
ngati ulibe dola kuno osabwera
macheza onunkha ife sitikulora
(tkeizz) vers
iwe tachoka nduka baller ndima baby a mtima ngati njoka
ma baby oti okhoza kuswela mtima uta shorter
with boys yongo spender as long as yonse iku ballеr
mix pachi friday sunday ndika b+n+r
might do it again the next day utiona
usayеse kuti crosser ase uziona
at least ukhale ndi ice ,if you wanna drip
ndimanjoya ngati ndi vacation ase i never trip
(hook)
Random Lyrics
- ifall - don't ask lyrics
- urbannino - herzbruchboogie lyrics
- joluxe - total annihilation lyrics
- jana kirschner - líška lyrics
- slamama - сhamomile lyrics
- godtearz - zatoichi lyrics
- lucille - crave lyrics
- skellyq - skolko lyrics
- sodom - hunting season (2024 redux) lyrics
- djeca! - želim s tobom sve lyrics