kwemogoon - ineyo lyrics
[intro]
[?]
[chorus: kwemogoon & kingdolla]
kakuti kathozipha chif+kwa cha ineyo
geliso kusiya chif+kwa cha ineyo
kathawaso kwawo chif+kwa cha ineyo
kati kathobwera ku show chif+kwa cha ineyo
kakuti kathozipha chif+kwa cha ineyo
geliso kusiya chif+kwa cha ineyo
yeah+ah, kathawaso kwawo chif+kwa cha ineyo
kabwera ku show chif+kwa cha ineyo, yah
[verse 1: kwemogoon & _kingdolla_]
kak+ma talker zosezo, eh
panopa nde tapanga settle, eh
kulimba ntima ngati metal, eh
kufilitsana ngati tomato
kati kagoma nane ndikhale wake boo
ndikafuna ku trapper ndizikatenga ku stu’
tizapange tiana ka jessy ndi ka ju’
nde kamavunga emoji kundiyika mu mood
[chorus: kwemogoon & kingdolla]
kakuti kathozipha chif+kwa cha ineyo
geliso kusiya chif+kwa cha ineyo
kathawaso kwawo chif+kwa cha ineyo
kati kathobwera ku show chif+kwa cha ineyo
kakuti kathozipha chif+kwa cha ineyo
geliso kusiya chif+kwa cha ineyo
yeah+ah, kathawaso kwawo chif+kwa cha ineyo
kabwеra ku show chif+kwa cha ineyo, yah
[verse 2: kwemogoon & kingdolla]
she say she down for mе kathopanga chilichose (chili’, chili’)
olo ‘usiya geli bola ifeyo tikhale tose (eh, eh, eh, eh)
kamafila kwemo no lie
kamandiwuza ngamo each and everyday no lie (no lie)
kakuti sikangandisiye
kangofuna kukhala ndine
ndikamunda kafuna ndikalime
kabweleratu kati kazishala ndine
yah, yah, kangofila star
[chorus: kwemogoon & kingdolla]
kakuti kathozipha chif+kwa cha ineyo
geliso kusiya chif+kwa cha ineyo
kathawaso kwawo chif+kwa cha ineyo
kati kathobwera ku show chif+kwa cha ineyo
kakuti kathozipha chif+kwa cha ineyo
geliso kusiya chif+kwa cha ineyo
yeah+ah, kathawaso kwawo chif+kwa cha ineyo
kabwera ku show chif+kwa cha ineyo, yah
[outro: kwemogoon]
chif+kwa cha ineyo
chif+kwa cha ineyo
chif+kwa cha ineyo
Random Lyrics
- guy - don't clap . . . just dance (12 mix) lyrics
- safira inema - opo kowe kroso lyrics
- valerie june - with you - a sweet little love song demo lyrics
- ken nordine - burgundy lyrics
- cutthroat mode - i don’t wanna die sober lyrics
- thomas r moore - he lives lyrics
- shelby (fra) - moula lyrics
- laer xirtam - zu müde lyrics
- z (of firing squad) - i hate yo face lyrics
- псарня (psarnya) - псина (dog) lyrics