lexblez - kuthira kukhosi lyrics
(verse 1: nyutu+geji)
pano ine sindimakhala soba
utangochoka moyowu uli proper
mzanga ndi mowa naje sindimakusowa
mzanga ndi mowa naje sindimakusowa
daily muma shabini ndi gin green
naje yiwala za ring ring
no more marriage dream dream oyee
unandisiya m’ma stress kundimvetsa ka pain
kundiluzitsa fame sha sha
unandisiya m’ma stress kundimvetsa ka pain
kundiluzitsa fame sha sha
me nah need you anymore
please let me go
pano zilibwino sindifuna wina no
tandipatse ka shot ndithire kukhosi
barman hehehe
(hook: twin m)
woo wooo
unandisiya wekha iwe najere eeh ah
unkawona ngati sindingapeze wina
pano ndimangothira kukhosi
mzanga ndimowa
ndimangothira kukhosi
mzanga ndimowa pano
ndimangothira kukhosi (mzanga ndimowa)
ndapeza wina
mzanga wachikondi
(verse 2: lexblez)
ndipatseni shot
ndimenye ka sip
ndufuna ka gin ndi sipe
zakale zipite
pano ine za ma babe ayi
bola mowa kukhala m’ma high
lero ndili well ndikatherano komkono ku stereo
ndipatse utatu bwana alipira bill yo
pano ndikungofirano ngati radio ngati rediyo
she will see a n+gga like me ndimakhala busy ndima geez
chaku st++z
kuthira kukhosi
chomwe ndimaopa ine ndi vakabu
ndimawuyamba kukuyera mpaka mbuu
ndeno mundimvetse akazi
anandisiya yekha najere padeni
pano ndimangothira kukhosi daily
aah iwe najere tiye uko
shakaa shakaa
(hook: twin m)
woo wooo
unandisiya wekha iwe najere eeh ah
unkawona ngati sindingapeze wina
pano ndimangothira kukhosi
mzanga ndimowa
ndimangothira kukhosi
mzanga ndimowa pano
ndimangothira kukhosi (mzanga ndimowa)
ndapeza wina
mzanga wachikondi
unandisiya wekha iwe najere eeh ah
unkawona ngati sindingapeze wina
pano ndimangothira kukhosi
mzanga ndimowa
ndimangothira kukhosi
mzanga ndimowa pano
ndimangothira kukhosi (mzanga ndimowa)
ndapeza wina
mzanga wachikondi
Random Lyrics
- roh yun ha & cherry boy 17 - cu lyrics
- amg dolo - lone wolf lyrics
- izna (이즈나) - timebomb lyrics
- mïndcrümb önda βeat - cuncrëtë lyrics
- jamie rose - who said? lyrics
- nihmune - breaking news lyrics
- pink sapphire - 真夜中のポートレイト (mayonaka no portrait) lyrics
- spinte - джуcи пуси lyrics
- hammon - licenza di rubare lyrics
- salò (aut) - sexy sport clips lyrics