lil al, em el & 60 grams - umakwana slime lyrics
[intro: martin meke]
nde pali kagulu aka kodabwitsa
kamatchedwa ma slime, ati ma slime
ahh slime mentality, slime mentality
titanyamula tima cup tawo, ati basi k+matenga codeine kuphatikiza ndi sprite
azimwa azikhala high hmm?
ana opusa kwambiri
nde timakhalatu k+mavala zima trouser zazikulu
kenako k+mazikhwefulaso hmm?
aah!
ayo 1800
[chorus: lil al]
k+mvela nyimbo zanga
umakwana slime, umakwana
top fan ati amangomvera nyimbo zanga
umakwana slime, umakwana
ati zimakape ziku biter ma concept anga
umakwana slime, umakwana
[verse 1: em el]
yeah
diso langa lafira chif+kwa ndimabanda
kamwana kakundi rider ngati yokohama
ana ohitter ife kamapalasa mabwana
mumanama ma guy mumanama
[verse 2: lil al]
ndine dolo ngati madolo ali an zanga (yeah)
ndizitrapabe ndi gang yanga situdana (yeah)
vuto sine ngati gang yanu mulibe shasha
mulowe flee market mukazigulire mpasha (yeah)
[verse 3: em el]
kuposta nditatchena amangoti wow, wow
akuti “come give me d+ck right now, now
yеah, ganja yanga ndiya loud, loud
phone ili pa dnd ndangogweza sound
[verse 4: 60 grams]
street n+gga sindisekеlera zachibwana
ndimakonda zaza, drip ti ana ndi ndalama
kakungondi yan’gana ndakafunsa what’s up?
eko handle sindikupatsa number yapa whatsapp (whatsapp)
[verse 5: lil al]
ayy wasteman sangakhale nzanga wa ine
baddie a delete kaye ig kuti akhale mkazi wa ine
droppin’ every week ndilibe nazo za timing
za hard nthawi zonse ma opps zakudya rock climbin’
[verse 6: em el]
kakufuna chanel, kakuwona ngati mdala wake ndi ineyo
ati mpaka ndizikatengera ku hotel (hotel?)
kakufuna ku breezer ine ndakagulira doppel
ati “em+el will you please be for real?”
[verse 7: 60 grams]
i started trappin’ you boys ain’t for real
standin’ on business forget a deal is a deal
i ain’t stoppin’ till i got a palm jive and that’s good[?]
they be like “where you from” i be like my mothers womb
ma hater ndi sh+t ndimawatampa ku loo
ndima slimer overnight, tapanga set up chi stu
[verse 8: lil al]
yeah
ndakachotsesa nyimbo za aidfest ndi kineo (kineo)
mumanama ma guy, mumanama
faka , lil al, 60 grams ndi achina em el
umakwana slime, umakwana
umakwana slime, umakwana
[chorus: lil al]
umakwana slime, umakwana
umakwana slime, umakwana
umakwana slime, umakwana
umakwana slime, umakwana
[outro: lil al ]
sound god
umakwana
umakwana
Random Lyrics
- rain (비) - love story (0912......그 이후) (chinese version) lyrics
- yung icon - ynt lyrics
- kaoru sudo - さよならはエスカレーターで (sayonara wa escalator de) lyrics
- hussein2k - предсмертное (neardeath) lyrics
- sam omi - hungry rant lyrics
- даня неред (danya nered) - драмы (dramy) lyrics
- zbb, l1nexx - drill aviation lyrics
- athena skye - motorboat lyrics
- double experience - lightfall lyrics
- 장민호 (jang minho) - 살자 (let's live) lyrics