
lil al - kape! lyrics
[intro]
yo 14 you got another one
ha, hahahaha
lil alzizizo
[chorus]
kape! sangacheze ndine
nchif+kwa zikuyenda ndipo sizingasimphine
sungadizadwe kusiphe, kofwala kuti ndilabwe ndimafunika ndilipidwe
iwe tangowona umene ndayika
tangowona umene ndayika
sungandipose kutchena mukupepuka mafana muk+manyika
huh iwe, iwe tangowona umene ndayika
[verse 1]
belo sh+t ndungoweneka za mtika
ngati ndimamvana ndi rose wabho bho
koma ndi wa cash drip
kungofika pa malo aliyense akufuna andimenyetse sip
tungodripper wa mame sungatipeze tik+menya ma nip
zi ana zuziwa i’m him zungofuna zindidyetse lip
ndungokakisser nipple kenako ndikadye nipla
umaziwa yanga ija sindiphweketsa limbwa
[chorus]
kape! sangacheze ndine
nchif+kwa zikuyenda ndipo sizingasimphine
sungadizadwe kusiphe, kofwala kuti ndilabwe ndimafunika ndilipidwe
iwe tangowona umene ndayika
tangowona umene ndayika
sungandipose kutchena mukupepuka mafana muk+manyika
huh iwe, iwe tangowona umene ndayika
[verse 2]
nda dropper kwambiri ma guy mu game akubanika
ma trapper a ulesi onse nde ndik+maliza
ngati ulibe dollar ndiwe artist wokanika
feature price ndima charger ngati ndikukaniza (yeah, yeah)
anandi b+tcherko kale nde sindimgawatenge serious
kungomubweleka rack munthu wayamba kusanduka mysterious
ha k+machenjera ma kape atha kubela
atandi slima phone ndinawoneka ngati mfana wopepera
but i didn’t care mix ndinali mu club, chi mwana chimandigwedezera
kenako chikundinong’oneza “big slime ndimaku hopera”
ukamuuza boyfriend wanyuowani atakudyera mkaladi
[chorus]
kape! sangacheze ndine
nchif+kwa zikuyenda ndipo sizingasimphine
sungadizadwe kusiphe, kofwala kuti ndilabwe ndimafunika ndilipidwe
iwe tangowona umene ndayika
tangowona umene ndayika
sungandipose kutchena mukupepuka mafana muk+manyika
huh iwe, iwe tangowona umene ndayika
Random Lyrics
- oily bastard - spring lyrics
- aleaka - numeri lyrics
- acid ghost - no joy lyrics
- moonga k. - hold on! lyrics
- grace disgraced - the hope lyrics
- tv head - never be alone (ft. levi post) lyrics
- maz - circle lyrics
- kyotosdesire - miyazaki lyrics
- roots manuva - knee-jerk - japanese bonus track lyrics
- beta boechat - o salva-vidas do metrô lyrics