azlyrics.biz
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

langwan piksy – maloto lyrics

Loading...

verse 1
i saw mwana w-nga
what a cute baby
proud dad anzanga anamva mbebe
kusiyana ndi ana ena iye -n-li star
ndinagwada kuthokoza mbuye wodalitsa
tinapita tonse kukagula ma dyper
t-tagwirana manja pamalo panaipa
tinakula koma we were getting tighter
anthu otiyang’anan amadziwa
timaitha

nkhope yake inali brighter
thupi lake linali lighter
ndi nzeru anamudalitsa
anatengera ine osakaika

ndibwelere ndikagone (heh)
mwina ndingalote nso (heh)
ndingadzamukonde
bola udzandibalire iweyoo

chorus
ndinalota maloto otsekemera ine inde
mwana w-nga atafanana nawe nde nde nde
iwe
ngati ndisadzuke
usadzandikhumudwitse
poti mtima w-nga kukhala nawe wavomera

verse 2
pali ponse
anaoneka akalilombe
ena anakondwa ena sanakondwe
pawirife chikondi chinalipobe
sichinachoke

ndi za mbirimbiri
zotilepheretsa kukhala awiri
tiye tidzikondana mmene tiriri
kunja kuli njoka w-nga ndiwe basi
ndikudziwa ndi zotheka eh
kukonda iwe wekha eh
chibwana ndaleka eh
iwe mphete ndikuveka eh

sweetie iwe ndine
mphepo ingawombe tisasinthe
limodzi tiwoloka mitsinje
mpaka tikafike hey
oh babie

chorus
ndinalota maloto otsekera ine inde
mwana w-nga atafanana nawe nde nde nde
iwe
ngati ndisadzuke
usadzandikhumudwitse
poti mtima w-nga kukhala nawe wavomera

bridge
no pain no gain
kukusiya iwe no ways
ngakhale asakondwe
everything is gonna be okay

no pain no gain
kukusiya iwe no ways
ngakhale asakondwe
everything is gonna be okay yeah

chorus
ndinalota maloto otsekera ine inde
mwana w-nga atafanana nawe nde nde nde
iwe
ngati ndisadzuke
usadzandikhumudwitse
poti mtima w-nga kukhala nawe wavomera



Random Lyrics

HOT LYRICS

Loading...