macia - sikileti lyrics
[verse 1]
zoti anzanu akakulakwilani, k+masunga mangawa
ayi zitheletu
anzanga zitheletu
zomati ayi adzatifuna ndalama zawo zikadzatha
ayi zitheletu
anzanga zitheletu
poti sudziwa chimene chibwere pa mawalino
chimene yawe amamusungira ndi moyo
anzanga ndi moyo
[pre+chorus]
poti inu si yehova
inu si controller
tosefe ndife olengedwa
ndife olengedwa
[chorus]
musandilodze ine
musandide ine
musandiwope ine, ine, ine, ine
ine, ine, ine
koma iyeyo osunga sikileti
odziwa sikileti ya moyo w+nga
ya moyo w+nga ine
[verse 2]
kukhalira kuk+mbana
kukhalira kujedana
ati ka bongo kamodzi
hi+jеt m’modzi
zomwezi mpakanaso matama, yeah
amayesa mwayi zinthu zosathеka
ku mtundu wawo kulibe anachita cha nzeru
anachita cha nzeru
but them don’t know
m’mene timaweluzira ifeyo nsimene amaweluzila yawe
timatsitsa oyenera kukwera
timakweza oyenera kutsika
[pre+chorus]
inu si yehova
inu si controller
tosefe ndife olengedwa
yeah, olengedwa oh
[chorus]
musandilodze ine
musandide ine
musandiwope ine, ine, ine, ine
ine, ine, ine
koma iyeyo osunga sikileti
odziwa sikileti ya moyo w+nga
ya moyo w+nga ine
[bridge]
inu si controller
ineyo si controller
tosefe ndife olengedwa
tichepetse nsanje, nkhaza, kusunga mangawa
ndingachedwe nazo
[chorus]
musandilodze ine
musandide ine
musandiwope ine, ine, ine, ine
ine, ine, ine
koma iyeyo osunga sikileti
odziwa sikileti ya moyo w+nga
ya moyo w+nga ine
musandilodze ine
musandide ine
musandiwope ine, ine, ine, ine
ine, ine, ine
koma iyeyo osunga sikileti
odziwa sikileti ya moyo w+nga
ya moyo w+nga ine
Random Lyrics
- xfears - believe is nothing (nevermore cover) lyrics
- $boy86 - деньги , роботы , любовь (money , robots , love) lyrics
- basement's glare - puppet master lyrics
- theheadlights - the point lyrics
- lil jao - trap dos careca lyrics
- jaze - safari lyrics
- will mannay - rain lyrics
- me & u2 - divine see code lyrics
- migue - obvios no lyrics
- bobby billy - a comédia assassina lyrics