martse - ma luv lyrics
[chorus]
zama love ndukuwuzani, you can die (iwe)
tiyeni tizingomwa mowawu ma guy (yeye)
zama love ndukuwuzani, you can die (iwe)
tiyeni tizingomwa mowawu ma guy
awo akuwota sakudwala (ndukuwuzani)
zama love, you can die
kukanika kuphaka appetite (sikubwera)
zama love, you can die (iwe)
[verse 1]
tulo silubwera, chavuta nchani anthuni?
mtima mw+nga muli nkhondo muli zibawuthi
koma zomwe akupanga alamu anuzi
kundiyika under pressure pano pa town
i think apeza njonda, mwano okhaokha
ati chibwezi ichichi mwatsalamo nokha
ati atopa akufuna kuchoka
akuti tayamba kusiyana ngini zokonda
anavaya ku party ndi achina jane
ak+mana ndima yo odziwa [?]
kubwera kwa ineyo k+madzandimvetsa pain
kenako avekere kuti its just a phase
[chorus]
zama love ndukuwuzani, you can die (iwe)
tiyeni tizingomwa mowawu ma guy (yeye)
zama love ndukuwuzani, you can die (iwe)
tiyeni tizingomwa mowawu ma guy
awo akuwota sakudwala (ndukuwuzani)
zama love, you can die
kukanika kuphaka appetite (sikubwera)
zama love, you can die (iwe)
[verse 2]
halima adandawula za daudi
amakambilanaso ndi sharon
akuti kha’ngati wapeza mamie mu town
shirt ija yabwera make up wa brown
ak+manjanjanjanja, olo kundihaga
ati nsima ndisaphike akadya wakawaka
phone ijaso wayika ma password aja
kwatsalaku mumva kuti nditha banja latha
anapita ku ndi ma boys
umadziwa akakhala ndi achina royde
nkhani ya akazi imakhala chi topic
kwathu ndili nako ndithu i’m going
[chorus]
zama love ndukuwuzani, you can die (iwe)
tiyeni tizingomwa mowawu ma guy (yeye)
zama love ndukuwuzani, you can die (iwe)
tiyeni tizingomwa mowawu ma guy
awo akuwota sakudwala (ndukuwuzani)
zama love, you can die
kukanika kuphaka appetite (sikubwera)
zama love, you can die (iwe)
[verse 3]
kundidyetsa flas ndizingogwira bottle (bottle)
ndithu kuyipatsa moto
zondiswera mtima ndati ine toto (toto)
ndithu kuyipatsa moto
kundidyetsa flas ndizingogwira bottle
ndithu kuyipatsa moto
zondiswera mtima ndati ine toto
ndithu kuyipatsa moto
[chorus]
zama love ndukuwuzani, you can die (iwe)
tiyeni tizingomwa mowawu ma guy (yeye)
zama love ndukuwuzani, you can die (iwe)
tiyeni tizingomwa mowawu ma guy
awo akuwota sakudwala (ndukuwuzani)
zama love, you can die
kukanika kuphaka appetite (sikubwera)
zama love, you can die (iwe)
Random Lyrics
- "coot" grant and “kid” wesley wilson - come on, coot do that thing lyrics
- vi3e - intro lyrics
- boy wonder (sk) - 2. šluk lyrics
- nad sylvan - crime of passion (vampirate’s anthem) lyrics
- call me schosa - brick and mortar lyrics
- yvng dyxrd - движем (moved by) lyrics
- haloo helsinki! - reiviluola lyrics
- leleee - gsr lyrics
- skyler day - a frame lyrics
- brymo - ọkùnrin mẹ́ta (ẹ̀dùn ọkàn) lyrics