mista gray - munthu wamba lyrics
verse 1
am a low g ngati hippo
ahh (eya tilipooooo)
peculiar people
nyali yapadziko sindichita mantha ndipo/
ndimadziwa christu yesu +n+lipila dipo/
sine wagwamba opanda g
sinditekeseka nnaima pa mtanda nji
namondwe chilala
ife, sitiima ngati ilala
zapadziko ndi zinthu zopanda phindu
sife michira ndife mitu ndithu
ndikuuzilenitu kuli christu ndi kwithu
ndima gainer confi nkati bible ndiphande
nkona pakamwapa pakula ngati chipande
kuspita zokomaku tafuna ngati dandy
sitinyinyilika monga ku ntchito pa monday
mboba ! odzodzedwa ndi mzimu osati komba
sober ! ehh ndili pa duty ndine khobha
zoba! ndimafuna pa den chamma 4 bar
wathu udobadoba sitivalila zigoba
chorus
a mi di eagle mi fly
greatness run inna mi blood
son a god heaven a min yard
mi a salty mi a gwan season di eath
koma sine (munthu)
koma sine (wamba)
moyo w+nga opanda malire
koma sine (munthu)
koma sine (wamba)
moyo w+nga opanda malire
sindingadzale chimanga ndikukolola tomato
kuti uyende upalase life ili ngati bwato
kugwa kudzuka kuyamba k+menya battle
ambuye akuti tidzaponda zinkhanila ndi nsato
opondeleza pansi mdzikoli achulukamo
ndavala ephesians 6 gospel ndi nsapato
faith ndi chishango, mchuno belt wa chilungamo
mau ake ndilupanga kuphwanya tonse mwatchelato
ukazamva fela ana blacka ndi mmene ndilili ndinadzadzidwa ndi mzimu
ndizinthu zondivuta kukhala gangster sinanga kutsaya kunadzadzidwa ndi chim
kukhala normal nono chi rapper chamakono
pa beat sitisiyapo phazi koma mlomo/
muzazing’ono zikh0m+ zogwesa nkhongono
ndimapinda bondo yesu k+muuza zikomo/
ndi mkokomo waziso tathyola kh0m+
muuze suffi tsono kuti nafe tilimommo
ehhh kukhala kape nthawi zina ndiudolo wazizur
we are di uncommon people
jah jah pickney we nuh lose like steven seagle
all di eyes on wi because wi cyaa be hidden
city pon di hill, eternal life we are given
sine munthu wamba utha kuyesa ndimatamba
ngini yomwe ndimapanga ndiyak+mwamba
high high ngati chamba
to all a dem king and queen wagwan!
alluwa (all who are) nuh cheap something wagwan
chorus
a mi di eagle mi fly
greatness run inna mi blood
son a god heaven a min yard
mi a salty mi a gwan season di eath
koma sine (munthu)
koma sine (wamba)
moyo w+nga opanda malire
koma sine (munthu)
koma sine (wamba)
moyo w+nga opanda malire
Random Lyrics
- edwin arzu - euphoria lyrics
- lous and the yakuza - maggie lyrics
- cmhd - back to back lyrics
- ill $werve - i never smile lyrics
- khalifah - salam aidil fitri (2020) lyrics
- phoebe katis - let me lose you lyrics
- udo jürgens - der sommer ist schneller vorbei, als man denkt lyrics
- f.o. & peeva (mitevi) - kvartala lyrics
- jax b€n - truth. lyrics
- andri dharma - salam barayo dari minangkabau (feat. kintani) lyrics