azlyrics.biz
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

mista gray - pa minga lyrics

Loading...

chorus

mwaiponya paminga game
mwaiponya paminga game
mwaiponya paminga game
ambuyeeee paminga game

mwaiponya paminga game
mwaiponya paminga game
mwaiponya paminga game
ambuyeeee paminga game

verse 1

all the praises to you
adatelo atagoma nanu mluya
game mwaiponyela kwa kuya
nkona ndikuimba hallelujah hallelujah

ndinu tate palibe ti to tu
tate mwana ndi mzimu is equal to
mulungu mmodzi wamoyo mwandichokesa
kutali madalitso double double ngati ma single two

school, banja, ntchito, business
abale anga chuma ndichibwenzi
mwaziponya pa nthambo yamagesi
adani sak-maka akuopa kugwidwa nyesi

sindipembeza zosema ndithabwa
ankandinyoza pano sakunditha bwa?
ndimayenda ndi mbuye wazatheka bwa?
i’m on my beautiful feet tangotcheka m’bwaa

chorus

mwaiponya paminga game
mwaiponya paminga game
mwaiponya paminga game
ambuyeeee paminga game

mwaiponya paminga game
mwaiponya paminga game
mwaiponya paminga game
ambuyeeee paminga game

verse 2

zikomo zikomo zikomo
zisomo zisomo zisomo
zandidutsitsa ineyo nzikh0m-
amene ali nkati mwaineyo ndi biggie kuposa alimu dzikomo

ena akudabwa ati ndicha
salary ya primary teacher
k-maoneka chimwana cho jintcha
ndi freestyle yomwe akufuna kupanga feature

zochimwa zanga mwazifufuta
misonzi yanga mwaipuputa
mwandidzodza mafuta, ndinudi chauta pamaso pa adani mwandidyetsa ndakhuta

munavekedwa chaminga chisoti
kukwapulidwa zikoti
ndisakambe zambiri chilungamo ndi choti

chorus

mwaiponya paminga game
mwaiponya paminga game
mwaiponya paminga game
ambuyeeee paminga game

mwaiponya paminga game
mwaiponya paminga game
mwaiponya paminga game
ambuyeeee paminga game



Random Lyrics

HOT LYRICS

Loading...