mufrika - kumpeta milombe lyrics
ooh ku mpeta milombe
kwathela ayamata ooh
ku mpeta milombe
kwathela alumbwana
ooh ku mpeta milombe
kwathela ayamata ooh
ku mpeta milombe
kwathela alumbwana
kuzebenza tisebenza bwino
ndalama timapeza
koma potsilizira pake eeh!
tinali nao anzathu
tinali kuseka nao
tinali nao astikana
odsziba kusamba bwino
nanga lelo alikuti
ambuye mwatisiyiranji
ooh ku mpeta milombe
kwathela ayamata ooh
ku mpeta milombe
kwsila alumbwana
ooh ku mpeta milombe
kwathela ayamata ooh
ku mpeta milombe
kwasila alumbwana
iyi nthenda niyoipa
ndiponso siyimasankha
imagwira aliyense
kuyambira kubana mpaka makolo
koma anyamata ndi astikana
nibame bakula maningi
nangatu tizakhala bwanji
popeza ndiye tsogoro
ooh ku mpeta milombe
kwathela ayamata ooh
ku mpeta milombe
kwathela alumbwana
ooh ku mpeta milombe
kwathela ayamata ooh
ku mpeta milombe
kwathela alumbwana
Random Lyrics
- cheez punk - первый (first) lyrics
- worm quartet - boning away on the ottoman lyrics
- dreamd - ждала меня (waited for me) lyrics
- quartetto cetra - una canzone per noi due lyrics
- naviroc - marietta 2 lyrics
- meimuna - voyage voyage lyrics
- humayun emerald - trappic lyrics
- poppa wafer - comeuppance lyrics
- tysare - bad influence (feat. zay!) lyrics
- pepel - в чём сила? (what is the strength?) lyrics