ngozi family - atate lyrics
[verse 1]
popita ku nchito a ibala to siya
ndalama ya chakudya pa nyumba
ngati ba choka ku nchito
ba pitila to bar
balezela moba wa 10 kwacha
pobwela ku nyumba ati iwe mukazi w+nga
nipase vi nsima na vi ndiyo
amai nabo ati imwe mulibe ku siya ndalama ya chakudya pano pa nyumba
atete iwo a yamba to kalipa
avula ma jacket ati nizaku lungiza iwe
[chorus]
a+a+atate lekani k+menyana ndi akazi atu
a+a+atate lekani k+menyana ndi amai atu
a+a+atate lekani k+menyana ndi amai atu
[verse 2]
please atate lekani ku chita ndeu
ine sindifuna ku menya amai anga
popita ku nchita mosaibala ku siya
ndalama ya chakudya pa nyumba
chif+kwa ntau ina ana onse
azankala ndi njala pano pa nyumba
amai nabo akati ayanguleko imwe mwa yamba ku bachita ndeu
[chorus]
a+a+atate lekani k+menyana ndi amai atu
a+a+atate lekani k+menyana ndi amai atu
a+a+atate lekani k+menyana ndi amai atu
[intrumental]
[chorus]
a+a+atate lekani k+menyana ndi amai atu
a+a+atate lekani k+menyana ndi amai atu
a+a+atate lekani k+menyana ndi amai atu
Random Lyrics
- ləman ömər - sənin olsun lyrics
- centaur - fields lyrics
- sonixxx - белым (white) lyrics
- pozer90 - ключі (keys) lyrics
- girls on fire (걸스 온 파이어) - dirty cash lyrics
- kleks - przejdzie deszcz lyrics
- scellé123 - europe lyrics
- mimmi bangoura - imaginary lyrics
- oswaldwalkemdown - pandabuy perc lyrics
- артём нефтяник (artyom neftyanik) - там-сям (tam-syam) lyrics