praise umali & faith mussa - chimwana changa lyrics
[intro]
mayo! chalowelera! (chalowelera dele!)
mayo! chimwana changa dele, mayo! chalowelera (chalowelera dele!)
mayo! chimwana changa dele, mayo! chalowelera! (chalowelera dele!)
mayo! chimwana changa dele, mayo! chalowelera (chalowelera dele!)
mayo! chimwana changa dele, mayo! chalowelera! (chalowelera dele!)
mayo! chimwana changa dele, mayo! chalowelera (chalowelera dele!)
[verse 1: faith mussa]
mwana w+nga ukupita (iwe! iwe, iwe)
chimwemwe ndi chisoni (iwe! iwe, iwe)
zagwira mtima w+ngawu (iwe! iwe, iwe)
times are bad and we know that
pamene ndingoyimba
[chorus: faith mussa]
(mayo! chimwana changa dele, mayo! chalowelera!)
iwe k+makapemphera uko (mayo! chimwana changa dele, mayo! chalowelera!)
sinkufuna kuzalira mwana w+nga ine (mayo! chimwana changa dele, mayo! chalowelera!)
osati chalowelera dele (mayo! chimwana changa dele, mayo! chalowelera!)
ndati k+makapemphera uko! (mayo! chimwana changa dele, mayo! chalowelera!)
usakalowelere (mayo! chimwana changa dele, mayo! chalowelera!)
[verse 2: praise umali]
k+mene ukupita uko (iwe! iwe, iwe)
iwe ukadzasochera ah (iwe! iwe, iwe)
mh mwana w+nga follow the light (iwe! iwe, iwe)
iwe follow the fire
pamene ndikuyimba
[chorus: praise umali]
(mayo! chimwana changa dele, mayo! chalowelera!)
mwana w+nga don’t forget to pray (mayo! chimwana changa dele, mayo! chalowelera!)
i don’t wanna lose you (mayo! chimwana changa dele, mayo! chalowelera!)
iwe udzikapemphera uko, iwe k+makapemphera uko (mayo! chimwana changa dele, mayo! chalowelera!)
[outro: faith mussa]
papapa (mayo! chimwana changa dele, mayo! chalowelera!)

iwe k+makapemphera uko
osati chalowelera dele
Random Lyrics
- smas - mojona tristona (scrapped track) lyrics
- 蘇打綠 (sodagreen) - 面面相覷 (face the situationship) (live) lyrics
- gutta - skydweller lyrics
- زالكا - enta el sabab - أنت السبب - ghassan (egy) - غسان & zalka (egy) lyrics
- kiesza - it's my birthday lyrics
- aphonnic - azúcar de algodón lyrics
- f-nix - cypher sobre cenizas: tobi lyrics
- 808eight & nine vicious - slime yo ass lyrics
- elxi - shake the sky lyrics
- iron flat - summer came twice lyrics