rapsean - kettie lyrics
artist: rapsean
song: kettie
intro
(t.h.a.m.a on the beat)
(koma rapsean adha iheehe)
i need your love on me(s.a media)
i need your love on me(kettie)
i need your looooo(ah)oooove(ah 2k production ihmm)
(koma adha)i need your love on me(kettie nayenso ah)
i need your love on me(ma frussi phwiiii)
i need your love on me
i need your looove
verse 1
tsono iwe kettie kodi chikondi amatero?
nnagwira 2010 koma kiss mpaka lero?
oro hug naye mwayi tinawombana munsewu
naponso unandikakha ngati timachita ndeu
ukundilora unkandifunadi kapena unkandiyesa?
nanga bwanji chilichonse ndumachita kukakamiza
nthawi inayake nd-nkaona ngati mwina ukunditiza
sukuchita bho zafikapa ukundikhiya
umandidyetsa mafruss ingakhale njala ndilibe
sikuti umandikonda ukandifuna credit ulibe
zoti ndimafuna chikondi ndine munthu mwaiwe mulibe
komabe nmakukonda sikuti ine ndili ngati iwe
hook
sindudziwa kuti ndiwe wotani
komabe umandidwalitsa mtima kettie
we been datin’ for really a long time
but i don’t see your love & i don’t know your love
sindudziwa kuti ndiwe wotani
komabe umandidwalitsa mtima kettie
we been datin’ for really a long time
but i don’t see your love & i don’t know your love yeah
verse 2
okongola sanyada akuluakulu anatero
iweyodi ndi ka nkhw-ngwa nkuona umanyada chotero
inetu kundiwazaku mpoti unanyasa bwino
nkhope ilibe ntchito bola mbina ili bwino
ndeno ndumadzifunsa,mwina nnanyasa kwambiri?
nanga zukhala bwanji ndi iwe wemwe nk-mandivuta
anzanga onyasa mondiposa onse anagwira
nde ine zuvuta pati?,mwina nkuti anandilodza
hook
sindudziwa kuti ndiwe wotani
komabe umandidwalitsa mtima kettie
we been datin’ for really a long time
but i don’t see your love & i don’t know your love
sindudziwa kuti ndiwe wotani
komabe umandidwalitsa mtima kettie
we been datin’ for really a long time
but i don’t see your love & i don’t know your love yeah
verse iii
penapake nmangofila ngati nngokupatsa mbama
chif-kwa sinchiona chomwe uchitira matama
ikakhala ya mapadi umadzatenga kwa ine ndalama
komabe sundilora kuti nchiteko zadama
penapake kudzifila choncho umachita bwino
chif-kwa ntakubonza chitha kungothera pompo
oro ntakupatsa mimba sungaione yasobo
ndipo mwana atabadwa iwe sungaone sopo
umandisowetsa zochita mpaka nmangobwira sugar
pena ngati mbuli ndimakasewera njuga
chif-kwa sundilora kuti ine ndidyeko juga
umwari wako khala nawo ndipeza ka judah gaga
hook
sindudziwa kuti ndiwe wotani
komabe umandidwalitsa mtima kettie
we been datin’ for really a long time
but i don’t see your love & i don’t know your love
sindudziwa kuti ndiwe wotani
komabe umandidwalitsa mtima kettie
we been datin’ for really a long time
but i don’t see your love & i don’t know your love yeah
outro
with all that i’ve said to you
i need your love on me
i need your love on me
i need your looooooooove(ah 2k production iiiih)
i need your love on me
i need your love on me
i need your love on me
i need your looove
Random Lyrics
- caleb slade - victory in defeat lyrics
- mars (producer) - darkest paradise lyrics
- kvr - i cannot believe it has come to this lyrics
- lady gaga - do what u want (kronic remix) lyrics
- cameran nelson - almost you lyrics
- gionni gioielli - sasha grey lyrics
- nowa - misshy lyrics
- key glock - orville redenbacher lyrics
- vanesa martín - el amor no se explica lyrics
- kim larsen - dreamer lyrics