ritaa - mubwere lyrics
ritaa mubwere lyrics
oh, sispence, oh oh oh
ritaa.. h+llo?
(verse 1)
munachoka kuti mukukasaka ndalama
mpaka lero simunabwelerenso
munachoka kutisiya ndi amai athu
koma simunabwelere..
simumatumizanso chithandizo kunyumba
koma zoti mukuchita bwino tik+mva
sitimadziwa ngati mumatiganizira
sitimadziwa ngati mumatik+mbukira
(chorus)
mubwere kunyumba
mubwelere kunyumba
mubwere kunyumba
mubwelere kunyumba..
(verse 2)
tinakula, otilera +n+li mai athu
kuvutika pamodzi ndi amai athu
komanso mutangopita
achimwene anatisiya
ana anu akungolira
chilichonse kuvutikira
phone yokha mukanatiimbira (h+llo?)
kalata yokha mukanatilembera (you know)
sitimadziwa ngati mumatiganizira
sitimadziwa ngati mumatik+mbukira
(chorus)
mubwere kunyumba
mubwelere kunyumba
mubwere kunyumba
mubwelere kunyumba
(bridge)
ohh, mubwelere kunyumba
oh, oh , oh ..
mubwelere kunyumba
(chorus)
Random Lyrics
- super beaver - まだ (not yet) lyrics
- node x larry 44 - lad det gå* lyrics
- babi xavier - baby, não pare lyrics
- slchld - instant lyrics
- zoe sky jordan - soft reply lyrics
- gerbia - toute m’énarve lyrics
- daniel band - running out of time lyrics
- mags (dnk) - elephant in the room lyrics
- chaostruppe - gold chain lyrics
- lia shine - sativa lyrics