azlyrics.biz
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

roosmac - drug lyrics

Loading...

usanditenge ngati kape, ukandiwona phee

zachibwana ndapangapo, mnawona kuti njee

all this love sh+t got me feeling all stray

zikavuta bola kupeza moto uwothe

chikondi chimakoma, until your heart is broken

mwana wabwino bwino eti mpaka wasochela

tima card ndizithunzi zonse afuna awotche
(yeaaaa)
k+mangolira osaphaka mpaka whole day
(yea)

am not a sober man, i drink all day

inu zikondani, ife tikonkhe

palibe vuto my n+gga it’s okay
(palibe vuto my n+gga it’s okay)

(yea)
i know the feeling
(i know)
been in the feeling
(yea)

it’s not a healing
(ase)

it’s only k!lling n+gga
(it’s only k!lling n+gga)

it’s only k!lling
(yeaa)
its only k!lling lovers

(flexem)

love is a drug

is a drug
(is a drug)+2

love is a drug
(is a drug )+2

chikati

chikubalalitse
chikati chikusinthile
(eeii)

love is a drug
is a drug
(is a druuuug)

ma overdose
(haahaa)

iwe ukazitengela

pena mk+mati bola kukhala wekha
(owwoh)

first time kuk+mana

mumakhala muli mtika

even her smile ngati sikazasinthika

kuwona man wonso

ngati kuti saza cheater
haha(check check)
osazitengela zingakome zingakome

k+mayiwelenga (uzabalalika nazo ase)

ukazitengela

chikondi ndi mankhwala ase

chikondi ndi mankhwala ase

amabwera ndi zawo

you better focus on yourself

mfundo zake zof++ka

she got me asking what ya say?

love takes you too far+25+

mpaka kufika manase

nkhani yake yamwane ase

love is a drug

is a drug
(is a drug)+2

love is a drug
(is a drug )+2

chikati

chikubalalitse

chikati chikusinthile
(eeii)

love is a drug
is a drug
(is a druuuug)

[love is a drug

is a drug
(is a drug)+2

love is a drug
(is a drug )+2

chikati

chikubalalitse

chikati chikusinthile
(eeii)

love is a drug
is a drug
(is a druuuug)]



Random Lyrics

HOT LYRICS

Loading...