sage poet - compassion lyrics
[chorus: game plan]
ndine munthu, dziwa ndiwe munthu
dziwa mulimatsonono kukoma
m’chikondi ndi anthu
mwamavume chikondi k+manga
osamakankhana tikhale mu chikondi, chikondi
[verse 1: tadala]
ey yo sage! popanda chikondi sindingakhale
ndingokhala ngati mtengo oti siungabale
ukakhala opanda mano siuswa phale
chisankho ndimakonda w+nkulu ena burley
ena amakonda kukonda ena kukondedwa
idzamera ndi mbewu yapa nthaka or yopondedwa?
nsambi kwa wa nsembe nsambi kwa m’levi
dzuwa sungazembe atelo ndi mlengi
atelo alembic ndikukonde ngati mwini
ngakhale ukonda ngini zopanda mwinimwini
wadyela koma wa mabala mu usinini
komabe mitima kutipula chikondi ndikufesa
zoipa kubzikula mwazi sindikukhesa
kufunsa mafunso ngati sindik+mvesa
mesa zikakuchulula zimavuta k+meza
[chorus: game plan]
ndine munthu, dziwa ndiwe munthu
dziwa mulimatsonono, kukoma
m’chikondi ndi anthu , mwamavume chikondi k+manga
osamakankhana tikhale mu chikondi, chikondi
[verse 2: sage poet]
the omnipresent love is above so below
because light is the electromagnetic in its form
love is alive from the moment we are born
from the womb to the tomb these are lessons we should know
it keeps us warm, sometimes the love is cold
light creates and breaks the patience in the soul
it’s in the heart, light is what designs in mind
love does not discriminate, light has always been the kind
god universal, ruler universal law
so, no matter who you is, light has balance of its own
it’s unconditional receive with no judgment
it’s compassion over others it’s the universal coven
light workers coz love nurtures us to the oneness
so, the path of devotion to open to door to abundance
it’s not far love is not a distant star
light is anuk ausar, god is love that’s who we are
love…
[chorus: game plan]
ndine munthu, dziwa ndiwe munthu
dziwa mulimatsonono kukoma
m’chikondi ndi anthu
mwamavume chikondi k+manga
osamakankhana tikhale mu chikondi, chikondi
[verse 3: sagonjah]
mulungu ndi chikondi ,chikondi ndi mulungu
zin+z+ zipembezo anakonda munthu
chikondi ndikukonda osasankhana ntundu
chikondi ndikukonda osawonana khungu
chikondi, lamulo la mulungu li modzi
mukonda bwanji mulungu ngati simokonda umodzi
zonama, chikondi sichikukamba zogawa
zomanza, chikondi chikukamba zomanga
chikondi, wadala okondedwa wakonda
kusiya kuwona chikondi ndichokongola
chikondi chilibe chilendo sichimaphonya
ngati unakhumudwa ndi chikondi chinali cha boza
chikondi ndi cha ulele, ndi cha ulele
[chorus: game plan]
ndine munthu, dziwa ndiwe munthu
dziwa mulimatsonono, kukoma, m’chikondi ndi anthu
mwamavume chikondi k+manga
osamakankhana tikhale muchikondi, chikondi
Random Lyrics
- tedonthebeat - whole lotta ted 2 lyrics
- hexecutor - burried alive with her white silk dress lyrics
- dary hezz - lo lograre lyrics
- bbahn - 이대로 좋아 (i like it) lyrics
- seven lions - rush over me (seven lions 1999 extended mix) lyrics
- jack mansion - this girl does not exist lyrics
- abbe may - freedom lyrics
- yelo [k-pop] - night sky lyrics
- o.c. smith - if i leave you now lyrics
- elle vee - stuck on repeat lyrics