
sagonjah & tadala - nthawi lyrics
Loading...
[verse: tadala]
ukunyeka wa uwisi uzatani owuma
sakuwakuwa ndi galu oluma
nthawi ndi mambala, mankhwala
nthawi imakwilila mabala
tizaona pa mawa
zikapola
nthawi ikapyola
mafuta owalitsa ndikazola
misonzi mtima kusweka
maso ku nyeka abwenzi kuseka
dziko kunyenga
nkhondo pachibale
mpeni muchidale
oyenda naye ndiyemwe amakutchela ndale
yeah ndikudziwa ali pompa yudasi
kunalembedwa nde ndilibe nthumazi
sizingasinthe
siungazithe
mmene zilili ndi milili itatithe
nthawi kukana nthawi kulola
si nthawi yotaya,ndi nthawi yotola
Random Lyrics
- rendom - ispred kina kulture lyrics
- von arroyo - mahal pala kita lyrics
- rich amiri - shadows lyrics
- mellie & n1face - выебываюсь (viebivaus) lyrics
- say she she - wrap myself up in your love lyrics
- benny dayal & monali thakur - jhilmil piya lyrics
- the rifftones - fine lyrics
- aegis - tell him lyrics
- rae sillycon - dummy lyrics
- apocalypsis - war money lyrics