sagonjah & tadala - saimba ng'oma lyrics
[intro: sagonjah & kim of diamonds]
tsararam tsara
saimba ng’oma, saimba uuuhh uuh
[chorus: sagonjah & kim of diamonds]
saimba ng’oma, saimba ng’oma
saimba ng’oma, saimba
wakula watha, wakula watha
wakula watha, wakula
saimba ng’oma
[verse 1: tadala]
satsogoza mthenga mavuto akamadza
mtima sandusa balaza mu bongo angozaza
ekhaekha angodweza mutu wqngofasa
ekhaekha angolakhula zi nkhawa kusanza
limenelo ndiye dziko mwakula
limagiligisha limamanga nyakula
kaya umapemphela umapanga maula
pena zitenthe ngati uli kunsi kwa mbaula
za chinyengo chidule
shatta sungapindule
dziko limakuteleka usanaiphule
zilimbe kuvala,usamazivule
k+mbitsa podzala, asamazizule
kukacha kolola
suziwa mtima wa moto pakapsa tonola
njira yako londola ena osamangolondola
lila mtima uphwe chipite ukangotonthola
chidziwa mchipande powomola
[chorus: sagonjah & kim of diamonds]
saimba ng’oma, saimba ng’oma
saimba ng’oma, saimba
wakula watha, wakula watha
wakula watha, wakula
saimba ng’oma
[verse 2: sagonjah]
kulakwisa n’kamodzi kubwelenza nchikhalidwe
uzaphunzira mowawa,anthu amaveka zingwe
uuuh sitibhambatira za ini
ukatalika manja mapeto ake ukayidi
osayedyela mmaso uli ndi chisankho
kusata maloto ,kapena zilalako(koma)
kuchita bwino kulibe chidule baba
ofa manja sang+yinukhe ataaa
ufulu ndikuyima pa wekha
moni wa munthu osawuka ammati kupempha
udolo ndikukwanisa ndi zomwe uli nazo
timapeza mosiyana simpitsano
wapambana wapeza chochita
ndalama imadana ndimanja opinda
inde nyengo zako utha kusintha
pali magonizo pamapezeka njira
[chorus: sagonjah & kim of diamonds]
saimba ng’oma, saimba ng’oma
saimba ng’oma, saimba
wakula watha, wakula watha
wakula watha, wakula
saimba ng’oma
Random Lyrics
- farruko, yung wylin' & maffio - good energy (remix) lyrics
- dmg 96 - szopa w pobliżu statku lyrics
- azahriah & desh - eldorádó lyrics
- 6occia - traffico lyrics
- joony - can't love lyrics
- release hallucination - anima lyrics
- kidd kawaki - künstlich lyrics
- pita said - winnen lyrics
- calvo el philarrican - por la window lyrics
- pearl charles - beginner's luck lyrics