sagonjah & tadala - zima lyrics
[chorus]
ndimakukonda
kukhala ngati kukulondalonda
sinkayika koma ndimawopa
wina azachuluka nzeru uzaf++ka
nkona
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati
[verse 1: tadala]
sindikayika
kuli mtima wako sikutalika
minga yachikondi mayo mtimawu wabayika
nde umaona ngati ndimakusata mapazi
ndikadekha ndekha jenkha manyazi
phone sumandiyankha ndimafoka
ndimafuna pena k+mandikankha
umatalikira
umatayilira
olo namondwe panyanja amakalipira
umandipilira
kupangitsa zinthuzi k+mapitilira
vundula madzi akhoza k+madikira
ndiwe w+nga komabe mtimawu umakusilira
madzi ak+mwa osamapisilira
sanje azikhala nayo mulungu ine ndi nda?
mwina ndikufunika uphungu nde tita?
sanje azikhala nayo mulungu ine ndi nda?
mwina ndikufunika uphungu nde tita?
[chorus]
ndimakukonda
kukhala ngati kukulondalonda
sinkayika koma ndimawopa
wina azachuluka nzeru uzaf++ka
nkona
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati
[verse 2: sagonjah]
mwina ndi mantha chabe
simmawupeza ndisaname
mwina m’mangawa simnachile ndimilandu yatizibwezi takale
mwina ndi mamuna wansanje
mwina, mwina ndi trauma
chikondi chandiwonetsa zowawa
pano [?] kuteteza mtima w+nga
koma mai mai kalanga
muzitaye zonse ine mmapanga
siine m’ngelo pena ukali
kaduka kuswaya chikondi kutali
koma ngati tingak+mane pakati
tonse tikubwеla kuk+mana mkati
zomwe ndipeleka ndi zomwе ndiyembekeza
[chorus]
ndimakukonda
kukhala ngati kukulondalonda
sinkayika koma ndimawopa
wina azachuluka nzeru uzaf++ka
nkona
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
[bridge]
zimakhala ngati
zimakhala ngati
nsanje
zimakhala ngati
zimakhala ngati
nsanje
zimakhala ngati
zimakhala ngati
nsanje
zimakhala ngati
zimakhala ngati
nsanje
[chorus]
ndimakukonda
kukhala ngati kukulondalonda
sinkayika koma ndimawopa
wina azachuluka nzeru uzaf++ka
nkona
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
Random Lyrics
- codeine kiss - polar lights lyrics
- wreckless eric & amy rigby - men in sandals lyrics
- rachel sweet - stick and stones lyrics
- dawnrooney27 - period lyrics
- star pvnk - aeiouy (vowels) lyrics
- azryl - radiant lyrics
- nine and dex - postman pat lyrics
- lil jaspy - western lyrics
- eddie and the getaway - crazy lyrics
- volob - вероника (veronika) lyrics