sagres 014 - awida lyrics
#intro [joskido]
dzina langa ndine bunda kulanga ana chipwete chalunda
kugawa chibhalo zibhalo year0 k+musiya paukapolo
kanyokhe kanyokhe komabe end ndidzakuyenda
simud+nkula afana mukule kaye mukali khanda chuh
#hook [sagres 014]
ndisanabwere pa bunda, nd+nkati ndidzayiphulah
mix pa den ka eight points nde nd+nkati ndidzad+nkulah
pano ma results now out portal ndukanika kutsekula
year0 ayinga apa zavuta apa nde mutu wakula
ndisanabwere pa bunda, nd+nkati ndidzayiphulah
mix pa den ka eight points nde nd+nkati ndidzad+nkulah
pano ma results now out portal ndukanika kutsekula
year0 ayinga apa zavuta apa nde mutu wakula
#verse 1 [sagres 014]
nditangobwera k+mene ndima leader life ya hiphop
mfana wa ding mfana wa llz wosemphsna nditi zikwapu
year0 ayinga apa zavuta apa nde mutu wakula
mid am on zеro end i don’t know apa asabula
mix chimfana cha llz nd+nkangodzimva u bnd
kudzuka mammawa kuvaya pa commoz pena kugona ku gmt
#cont….[temano]
yama badman eeh, portal kuopsa ngati ndе ndiku vatican eeh
acting very bad pa bunda ndine veteran, shaa!!!
mutu wakula kugoba frus but still on a front line yeah
feeling vibes mix nde timango dripper aise
anyani anyani nkati bola mpeze pap
reaching my goals
#hook [sagres 014]
ndisanabwere pa bunda, nd+nkati ndidzayiphulah
mix pa den ka eight points nde nd+nkati ndidzad+nkulah
pano ma results now out portal ndukanika kutsekula
year0 ayinga apa zavuta apa nde mutu wakula
ndisanabwere pa bunda, nd+nkati ndidzayiphulah
mix pa den ka eight points nde nd+nkati ndidzad+nkulah
pano ma results now out portal ndukanika kutsekula
year0 ayinga apa zavuta apa nde mutu wakula
#outro
awida
awida
awida, onse achina ida awida
onse omwa ma ryder ma cider awida
Random Lyrics
- stou rr3d - 9adech men mara lyrics
- paves 16 - heartbroken lyrics
- quezz ruthless - big scarr flow part 2 lyrics
- bachelorbby & jaspercd - anders lyrics
- pig - dirty mercy lyrics
- katya kudos - нексюша (janaz remix) lyrics
- scorey - party on the weekend* lyrics
- alex hopkins - good morning lyrics
- smokefullboy - dreamcore vibes lyrics
- yd yukki - bathe lyrics