seven-o-more - zonsezi lyrics
[intro]
yah
ya achina seven adah
[chorus]
ambuye amatikonda (yah)
mulungu amatikonda (yah)
chauta amatikonda (yah)
ambuye amatikonda (yah)
amatidzutsa tikagwa
amatichilitsa tikadwala
timuyimbile kuti izi+pitilile
[verse 1]
ambuye amakonda aliyense
mphepo imapeza aliyense
mvula imagwera denga la aliyense
dzuwa limapeza aliyense (yah)
onani munthu, onani mbuzi, onani nkhuku, mwanapiye, khwiyo
onani dzuwa, onani mwezi, chiphariwari khakhakhakhakha
+n+lenga zonsezi (yah)
+n+lenga nyanjazi (yah)
+n+lenga nyamazi (yah)
+n+lenga chambachi (yah)
ngakhale mdima ungakure bwanji padziko lapansi kunja k+machabe
ngakhale mvula ingavumbe bwanji padziko lapansi nyerere sizifa
+n+lenga manyazi (yah)
+n+lenga nsanjezi (yah)
+n+lenga nkhawazi (yah)
+n+lenga imfayi (yah)
+n+lenga chisoni (yah)
+n+lenga misozi (yah)
+n+lеnga chikondi (yah)
+n+lenga mtenderе (yah)
+n+lenga satana (yah)
anthu m’matsapana (yah)
anthu m’mangophana (yah)
ana ajaja wa (phrr)
[chorus]
ambuye amatikonda (yah)
mulungu amatikonda (yah)
chauta amatikonda (yah)
ambuye amatikonda (yah)
amatidzutsa tikagwa (yeah+yeah)
amatichilitsa tikadwala (yah+yah)
timuyimbile kuti izi+pitilile
[verse 2]
yah, yah, yah, yay, yah, yah, yah, yah
yah+yah, yah+yah, yah+yah, yah+yah
chopangidwa padziko lapansi, chimathela pa dziko lapansi
nkango wayuda sangalore, mpaka tsiku lina tizayimba++
mtendere (yah), mtendere (yah), padziko lapansi (yah)
yesu ndi mfumu yathu, ndi mfumu ya mtendere (oh my god, oh my god, oh my god)
mtendere (yah), mtendere (yah), padziko lapansi (yah+yah)
yesu ndi mfumu yathu, ndi mfumu ya mtendere, eh (oh my god, oh my god)
(yah, yah)
Random Lyrics
- anuel aa - anoche soñé lyrics
- venomssj - intro lyrics
- kevin (the boyz) - rubber boots lyrics
- dj pv - me llevas más alto lyrics
- cégiu - valediction lyrics
- lil' eggroll - why you mad? lyrics
- гесс (gess [rus]) & toby yams & ybf gotti sound - luv2 lyrics
- dimitri vegas & like mike - all i need (dvlm x bassjackers vip mix) lyrics
- 3d melz - run up a bag lyrics
- loganplayz - 1/3 lyrics